Vote For This Song
Lyrics
Sindikuti ndifa mawa, koma papsya tong'ola poti suziwa mtima wa ndalama Ndiye ndikazipeza pompo ndimazi spender Sindidikira kuti mawa kapena kuti kucha bwanji Poti sinziwa za mawa kuti kapena kudza bwanji Choncho mwina ndingazafe ndalama yanga ili mthumba "NO!" Chorus Umangoziwiratu iwe!Kuti ya ine ija (ija) Dollar siigona mthumba (siikhalitsa) Ikagona mthumba ndalama imeneyo ndi haraam (malodza) |
Songwriters
2 Street, KelzinSharing is cool
You may also like...
Mobile Site
Review
Comments

Songs By 2 Street Songs | Party Yama Rasta » |