Vote For This Song
Lyrics
Intro (Ayi ayi aii) Uwoo oh ooooh oo (A2121 MIT CROUZY & Trumel pon di place mi say) I miss you i miss you my lady Chorus -Alikuti Nasibeko mmangofuna ntangomuona, - Alikuti Nasibeko mmangofuna ntangomuona Nkhope yake yowala mm mmangofuna mtangoionaa - Thupi lake losalalaa mmangofuna ntangomuhoda,. (Verse1 A2121) -Ili ndi fuso lomwe ndalandila kuchokera kundendeko - Nkhani yomwe inamanga nthenje eh njokhudzana ndi Nasibeko, - Mchimwene analira momwe ndinamangidwira Nasibeko osadzandionako, -Ngati pali china chomwe ndinamulakwila mumuuze akhululukeko o - Ine jenkha ulephera kuyankha nkamba chani za Nasibeko, - Ndimati nkati mwina mwake nsokoneze nkhani wandifusa za Nasibeko oh,,, (Chorus Trumel) ( Verse 2 Trumel) - I'am deep in the dackness, - Kukhala moyo wa madness - am dying for your Caress - Cyaa wait (cant wait) to see your face (Listen) - Ndamusowa Jane ndi Junior, Ndidziwa nao asowa ineyo, - Ndikhala bwanji opanda iweyo, - Poti chikondi changa ndiiweyoo, - You don't know how much a wana get out of here, - A wana come down dear, - A wana see you ma dear (oo oh) (Chorus Trumel) - Alikuti Nasibeko mmangofuna ntangomuona, - Alikuti Nasibeko mmangofuna ntangomuona Nkhope yake yowala mm mmangofuna mtangoionaa - Thupi lake losalalaa mmangofuna ntangomuhoda,. (Verse 3 A2121) - Iyi ndi kalata yomaliza tawelenganii yomwe adasiya Nasibeko, - Dziko lopanda iwe nchimodzimodzi mtsinkho wa nkhwanii opanda nchere ndi Tomatoe, - Ana awiriwa uli ku ndende mlela ndanii nkhawa idagwira Nasibeko, - Tsalani bwino dziko lapasi lokonderalii ndatha ndine wanu Nasibeko. - M'banda kucha wina anthu olawilira - Anamupeza Nasibeko wadzimangilira - Anatikuwira mudzi onse unathamangira, - Mwatsoka tinakapeza Nasi wamwaliraa ah, (Conclusion) - Alikuti Nasibeko (Nasi anamwalira a) Alikuti Nasibeko (Nasi tinakwilira a) |
Sharing is cool
You may also like...
Mobile Site
Review
Comments
