Vote For This Song

Lyrics

Intro A2121 ee aaa aah ah Chorus Ichi chikondi ndichomasukirana ndichopanda madando sichopaka ma Tippex Or akwao sangabwere kwathu mkudzachita mavando chilibepo ma tippex Owo owo owo sichopaka ma tippex Owo owo owo chilibe ma tippex Ichi chikondi ndichomasukurana ndichopanda madando sichopaka ma tippex Or akwathu sangapite kwa mkukapanga mavando sichopaka ma tippex Owo owo owo sichopaka ma tippex Owo owo owo chilibe ma tippex, Verse 1 Chisankho chako mchanga chisankho changa mchako oo no mistake, Ndizifukwa zokwana ukuliyambe banjaaa tikadye biscuit,, Awo ankandikana pano akundikonda chonchi bwanji aika Tippex,, Asusukira otchuka chikondi chawo asinthitsa ndi ndalama ali cheapest,, Bridge Chikondi chaiwe ndiineyo ayi mchosapaka Tippex,, Ndipo iwe usankha ineyo ayi sudachite mistake,, Back to CHORUS, Verse 2 Chikondi sachonderera aliyese azimasuka sendera sendera, Asakupatse madandaulo mtima wako munchikondi ukhale okondwera, Narrow & void chikondi cha tippex, Chingauike moyo wako pa risky, Kukonda osakukonda dats a mistake,, Umukonde oti akuuze,,, Bridge

Sharing is cool

You may also like...



Mobile Site

To view this page on the Malawi-Music.com mobile site Click here

Review

Comments
Hits 13512 Plays. | 21349 Downloads.

Follow Malawi Music on Instagram