Vote For This Song
Lyrics
Undimamatile Lyrics (Verse 1) Usamakhumudwe dzikoli ndi choncho, usamafooke Moyowu ndi choncho, kulakwirana sikulephera, kususulana sikukanika mchikondi, chofunika undigwiritse undikakamile, Chofunika undigwiritse usagive msanga... (Hook) Ndimakukonda, Ndimakufiiila, nchifukwa chake ndinena..Undima..ma..ma..ma..ma..ma..ma..ma..ma..ma..ma..mati..lirebe iwe..Undima..ma..ma..ma..ma..ma..ma..mati..lirebe iwe eeeh.. Undimamatile ndikumamatile Undimamatile ndikumama.. mamamamatilebe iwee...Tikafika.... (Verse 2) Pena ndimalakwitsa kukulakwira mnzangawe Pena ndimachita zodzikonda kukuswerako mtima, koma.. kulakwirana sikulephera, kususulana sikukanika mchikondi.. Chofunika undigwiritse undikakamile Chofunika undigwiritse usagive msanga...(back to chorus) (Bridge) Undimamatile ndikumamatile Undimamatile ndikumama..mamamama... undimaaaaaaaa, Ndikumaaaaaaa...,. |
Songwriters
Astabo, OBKSharing is cool
You may also like...
Mobile Site
Review
Comments
