Vote For This Song
Lyrics
(Verse 1) Andy Musiq Oh oh oooh nah nah nah ye ye yeah Kachuma kanga konse ndimafuna ndikaononge..(Paiwe).... Chaka chino chokha ndimati ndikukwatile.. Ana awiri,atatu, odalitsa ukwati pope... Kaukwati ka international, osati za lokolo ( lokolo eeeeh) Koma chosadziwa ndaimbila mfiti m'manja Kumafetsa pa tanthwe nkumayesa ndipa nthaka Mano nditanola eeeh, nyamandikundibisira eeh Koma sunaziwe kut Chorus(Andy Musiq) Nali ndima plan inee (pa iweeh) Nali ndima plan inee (pa iwe eeeh) Koma vuto iwe wadya mfulumira, wadya mfulumira, wadya mfulumira kuchokaweh ×2 Verse 2(Saint) Ndinkafasa ine kuona tsogolo la mawa ndinkadekha ine Kufuna kuona maso ankhono Chikondi chinali cha nkhongono Ndinkati iwe uzandigwira nkono I had all my eyes on you I had vision for you Tsiku ndi tsiku kukulingalira dem real dreams for you Sindinkafuna kukuona ukulira I was damn serious, damn serious but u messed up see u messed baby Chorus (Saint) Ndinali ndi plan baby(pa iwe) Ndinali ndi plan inee (pa iwe) Koma vuto wadya mfulumira Wadya mfulumira wadya mfulumira Ndi plan ine, ndi plan ineeh Wadya mfulumira wadya mfulumira Wadya mfulumira iwe, iwe Verse 3 (BLAZE) Napepe mam mudachita phuma yeah (phuma yeaah) Mukadasankha Chikondi osakhala chuma yeah (chuma yeaah) Mudathamangira bwibwi kamba kazilako lako (lako) Pomwe chakumwa chanu mudali nacho m'manja mwanu (mamie yeah) Palibe chomwe nkanangopenya ndimaso anuwo (anuo) Chilichonse dafunitsitsa chikhale chanunso Mtima wazi lako lako (lako) Mtima osilira mamie aaah yeeeh Mwazionongera nazo banja Akome chotani mamuna amene mu laka laka eh yeah Chikhale chotani chikondi mufuna maka maka ayeeh Mbali yanga ndayesesa nkhale ndimayesesabe Koma nkutheka mamuna mufuna inuo sineyo Chorus (Blaze) Nali ndi plan ineee eh (pa iwe) Ndi plan ine eeh eeh (pa iwe) Mai-mai mai-mai ma yoh Ndi plan ine eeh eh Ndi plan aaah ah ayeah yeah Ndi plan, ndi plan, ndi plan ine eh eh |
Songwriters
Andy Musiq, Blaze, SaintSharing is cool
You may also like...
Mobile Site
Review
Andy Musiq, Blaze, and Saint link up on this new RnB song that's sure to shake up the airwaves.
Comments
35709 Plays. | 35557 Downloads.
« Ndekesha | Singles Songs | Usandisinthe ft Janta and Mwanache » |