Vote For This Song
Lyrics
INTROKubwera kwako mmoyo mwanga Ndazindikira ine kuti chikondi ndichokoma Akazi onse m’mbuyomu amkangondi user I regret now CHORUSUmachedwa kuti iwe M’mbuyo monsemu_ena amkangondiseweletsa mtima Unali kuti iwe Nthawi yonseyi_ndimkasowa chikondi chako Umachedwa kuti iwe M’mbuyo monsemu_ena amkangondiseweletsa mtima Unali kuti iwe Nthawi yonseyi_ndimkasowa chikondi chako VERSE ONENdinafika pongovomeleza ndikumati True love never exist Nanga chikondi chomwechi Wina akunjoya wina akumvetsedwa kuwawa Koma kubwera kwako mmoyo mwanga Kwandipangitsa_ndilimbenso mtima Koma kundikonda kwako iwe Kwandipangitsa ndichidzidziwe chikondi CHORUS
VERSE TWO
Kukonda ndimkakonda koma kukonda olakwika
Ndimkayesetsa koma zimkangovuta
Pena umakhala kapolo wachikondi
Kumamukonda koma osakondedwa
Gal u came in my life with a posibility
Wangobwera m’moyo mwanga chilichonse kusintha
Ndi iwe ndalimbanso mtima
Kukonda kwako pano ndikukamba zina
BRIDGE
One thing I know about love
Chikondi sichitengera experience
Chikondi ndimumtima take it easy osapnga phuma
BACK TO CHORUS
VERSE THREE
Wandionetsa kuwala chikondi chako chili ngati makhwala a moyo wanga
Iwe mkazi unafatsa you amaze me ndichikondi umandipatsa m’moyo mwanga ah ey
(ndichikondi umandipatsa m’moyo mwanga ah eey)
|
Songwriters
Battafly, Dj SleySharing is cool
You may also like...
Mobile Site
Review
Battafly links up with heavy hitter Dj Sley for this nice song. Enjoy!
Comments
34000 Plays. | 31549 Downloads.
« Ndayesetsa ft Nes Nes | You never know Songs | Munthawi Yake » |