Vote For This Song
Lyrics
Intro (Bathro) Matthew 24:29 KJV “After the tribulation of the days shall the days be darkened The moon shall not give the light And the stars shall fall from heaven” Verse 1 (Bathro) Ndangomva akukamba Ngakhale osuta chamba Pakamwa ndi polemba Dzikoli ndikumwamba Mfuulo ndi mawu Akuda ndi mashau Sizinasiye Mtundu Ngati moto woyaka Liwiro ngati zaka Ngati bomba losweka Kutembenuza nthaka Aneneri onyenga Komanso anamalenga Kufalitsa nkhaniyi Chorus (Wakisa James) Dziko likamazatha Lipenga kulira Zizakhala zowawa Ulibe Yesu mumtima Nzanga uzatani iwe Nzanga uzatani iwe Dziko likamadzatha Dziko likamadzatha Verse 2 (Bathro) Eti dziko lizatha Ngati moyonso umatha Ena kuthatha ndi mantha Kuvomera kwawo kwatha Ngati mdima opanda mwezi Kuzakhalanso zoopsa Kuganiza mozama Malingaliro mumtima Kufatsa ndi mafuso Ngati mwana osankhwima Kodi kuzabwera Gorzilla Mafumuwa kulira Ndi nkhondo zamumdima Ngati Hollywood vampires Chorus (Wakisa James) Dziko likamazatha Lipenga kulira Zizakhala zowawa Ulibe Yesu mumtima Nzanga uzatani iwe Nzanga uzatani iwe Dziko likamadzatha Dziko likamadzatha Verse 3 (Bathro) Mayi ubwere utatu Umwedwe wakwathu Akaziwa ndi forty Koma nditenga atatu Zikukoma chomwecho Zatulukira zilombo Ena ali kotamba Mankhwala akusamba Magamba akufwamba Ena mabodza kukamba Koma bwanji sitimamva Iyeyo adzabwera ngati mbamva Chorus (Wakisa James) Dziko likamazatha Lipenga kulira Zizakhala zowawa Ulibe Yesu mumtima Nzanga uzatani iwe Nzanga uzatani iwe Dziko likamadzatha Dziko likamadzatha |
Sharing is cool
You may also like...
Mobile Site
Review
Comments
