Vote For This Song
Lyrics
INtro: Blakjak,, Inde! V2... Haha,, Iwe! Tsegula Khomo Amjiba alowe ey Amjiba Afika,, Iwe Tsegula Khomo amjiba aloweeh Amjiba afika.. CHORUS Indetu Indetu Ndinena Ndi Iwe Tambala wachitatu asanalire Lero Lomwe, Ndikadya kunyumba Kwako Lero Lomwe, Ndikamwa madzi ako *2 VERSE ONE Iwe! Usandisiye ndili Chiimire Tabwera Uzandichi-chi-chi-chi-chi-chi Chingamire Poti ndato-to-to-to-to-to toperatu Komanso zonse zofunika ndaguliratu Bwanji ukakhala ngati sukukondwa? Kapena ukukayika zoti ndimakukonda? Iwe ndi ine mpakana kumanda ndipo ngati Piksy Mtima wanga Wamata.. CHORUS VERSE TWO Takawoneni Ka Mkazi Akoo Kowoneka bhoo, Kopanda tsankho Kakuti, Blakjak bwera tipange Chipako? Ndakawuza zimenezo upanga ndi Ambuyako Ati Blantyre Umakhala patipati?? Ndakauza Nkolokosa cha Mkatikati Akuti, How come you FAT but you Still SMART? Uzaziwona, ukazakhala Merchant. CHORUS VERSE THREE Akuti Akufuna chikondi cha Classic Watopa ku user zingini za Plastic She dont wanna Compromise her quality (hehe) Because she's Sexy and she knows it People asking, Chikwati Chiliko liti December Fanz ipange profit (haha) Umangotero Chaka ndicho chiti? Am like, zimenezo GOD knows it! CHORUS BRIDGE Tsegula Khomo Amjiba alowe ey Amjiba Afika,, Iwe Tsegula Khomo amjiba aloweeh Amjiba afika.. *repeat chorus then ends* ..thanks for your usual support |
Songwriters
Fatsani Michael Che-KalondaSharing is cool
You may also like...
Mobile Site
Review

« Mavuto | Indetu Songs | Leaving On an AXA Bus (Feat Zeze, Kenny Klips) » |