Vote For This Song
Lyrics
Intro: Nyimbo zoyimba usiku zimakhala inayake,, Mwana wakwa neba.... Snowky on the beat,, Mwana Waka Neba... Blakjak Inde Verse One: Dzudzuloli Kanabwera, pa den panga/ Koma katavala Mopelewera/ Ati ndimammbanda nkamasekelera (hahaha)/ Akufuna kundiberaa chani?/ Tangonena Zomwe Wabwerera/ 'Funa nzikagona Dzulo nnaledzera/ Akuti mhh, Dolla Yandipelewera/ Tandibwerekeko Mawa Nkubwezera/ Aaah Iwe, Mesa Dzulo ndakupatsa ina/ Nde leronso wati ukufuna ina/ Chabwino Ndamva pita Ubwere Nthawi ina/ Koma Chonde, usamuuze Georgina, Wamvaa? Chorus: Mwana wakwa Neba Chonde ndisiye, Undichimwitsa Ndaona Kale zomwe iwe Ukuchita Ndipo Ndazidziwa Komwe Zikupita Vuto Siine Koma Mwana Wakwa Neba Ndamuuza Chonde Undichimwitsa Ndaona Kale zomwe iwe Ukuchita Ndipo Ndaziona komwe zikupita Verse Two: Lero Kanabweranso kungofikira Kuchipinda Ati iwe Blakjak kodi eti Chipi ndi nda? Chipi..? Ndi Nzanga, bwanji akufunsa nda? Ndimangofuna akudziwa basi.. Nanga Linda? Basi Mafunso atha, usandifunse Zimenezo Usatsegule Pamenepo, Usandigwire Chimenecho Ukundiputa dalatu Zako zimenezo Si izi, Ine Nnadziwatu, Sizitha bho Koma ndakuona Ukukula Ndipo Mmanja mwangamu Ndakunyamula Ndiye lero ndikuwone Ukuvula Shaa,, Kumeneku si Kulaula? Chorus: Verse Three: Iwe Mwana wakwa Neba! Tabwera kuno Dolla yanga ija nanga bwa? Masiku akutha nde ndikudabwa Kuti Muzatibwezera, kapena basi Aah? Ati Eeh panopa Dolla Ndilibe Koma ndimakufira ndisakunamize Nde, Nditha kukupatsa choti Ugwirize Nkazapeza Dolla ndizatenga, Easy Ine kudabwa munthu wayamba Kuvula Thrauza Shaa! Ndithawe nkayitane ma bouncer Koma n'kathawanso Mfana Azaphwekesa Mapeto ake siizi,, Wandichimwitsa Eeh! Chorus: Repeat chorus then beat ends... |
Songwriters
Blakjak, Snowky SmokeSharing is cool
You may also like...
Mobile Site
Review
Comments
21682 Plays. | 26582 Downloads.