Vote For This Song
Lyrics
Intro: Blakjak,,, Inde! Mavuto, Ukutinyoza (Ukutinyoza?) Iwe ndiwe M'bale wa ifetu, Okay? Lets go..
Verse1 Mkwiyo wako wandipangitsa kumakutalikira Nkhawa yanga, sukundiuza chomwe ndakulakwira Ukumauza anthu ambiri ukundikayikira Kuti mkazi wako uja ndikumuzembelera Mavuto- waiwala komwe tikuchokera? Mkazi wakoyu si ine ndemwe n'dakugwilira? Of coz one day ankandisekelera but me didnt do nothing n'nali ntaledzera Chorus Ndayamba kale kukuyitana koma sukundiyankha Ndayamba kale kukuyitana koma sukuvomera Kodi nchani chenicheni chomwe n'dakulakwira Ngati n'dakulakwira, bwanji osandimasula? Chorus2 M'bale wanga mavuto-ziiiii M'bale wanga Mavu- ziiiiii *4 Verse2 Chomwe udziwe chibalechi chili ngati fupa Pena zimayenda boo, pena zimashupha Olo palibe moto utsi utha kufuka Takumbukira tikuvina Lupupa-Lupupa Haha- kuchipindako tatuluka Tiyeko tikamuone Francis Kaphuka Tamakhalani ngati munagera pa Kaphuka Tasekelerani, Misonziyo Pukuta. Chorus1 Chorus2 Verse3 Zili bwinotu apa mmene tili limodzimu Osati kumangokwiya ngati za mizimu Aliyense akungokamba za ife mmuzimu Akuti tikumamwa mowa ngati opanda nzimu Naye Mkazi wako uja walowa chisawawa Mfana aliyense otchuka n'taleka ntalawa Mma Facebook mmenemu fanz ikumunjoya And she is telling everyone ati samakusowa Chorus1 Chorus2 Bridge A wah dis me ah hear? Unuh talk 'bot me ah nyam yoh Empress deh? Ah why so? Cya a hug up, we ah hug up? Mavuto- Rudebwai, Get yuh Life deh Chorus1 Churos2 (song ends with beat) |
Songwriters
Fatsani Michael Che-KalondaSharing is cool
You may also like...
Mobile Site
Review
Indetu Songs | Indetu » |