Vote For This Song
Lyrics
Climax_Opanda Amayi[Motherless]Prodby W Music Entertainment( Lyrics)-2020 Intro Palibe chowawa ngati kukhala opanda Mayi!!(Conqueror!! Conqueror!! ))// Moyo umawawa ngati ulibe Amayi!!! (Climax to the max)// Moyo unakhala bwanji? ×2 Verse 1 Aaa! Life imakhala simple akakhala moyo Makolowa// Koma Ama akapita kumasowa Kholowa// Umayamba kutolatola ngati Mbalame// Step mother ndikuzachotsa ku Academy// Umalephela kugwila remote mene ukagwilila earlier// umatha kuchoka ku Urban to Remote area// Ndee!! akakukana Uncle// Umachita kusowa okugwila Ankle// Ana akulila.. Akulila!! (Akulila!!!!!! )// Palibe owa samalila!!!!! Hook Palibe Chowawa ngati kukhala Opanda Mayi( Opanda Mayi!! )// Moyo umawawa ngati Ulibe Amayi( Ulibe Amayi!!!)// Moyo unakhala bwanji?( Moyo!! Moyo!!) Moyo unakhala bwanji?( Moyo!! Moyo!!)// Nanga tidzikhala bwanji?(tidzikhala bwanji??!!... Motherless) Verse 2 Tikhala bwanji? Amami apita!!(aaa!!)// Tikhala bwanji? Adad apita!!(aaa!!! )// Tikhala bwanji? Azakhali apita!!(oono!! )// Tikhala bwanji? Malume apita!!!(onoo!!! )// Ine ndimadabwa!! Wina akamanyoza amama(Why Why Why)// Ine ndimadabwa!! Wina akamaphweketsa amama(Why Why Why)// Mwina samadziwa mene uwawila Umasiye// Mwina samadziwa!! mene uwawila Umasiye!! Hook × 2 Palibe Chowawa ngati kukhala Opanda Mayi( Opanda Mayi!! )// Moyo umawawa ngati Ulibe Amayi( Ulibe Amayi!!!)// Moyo unakhala bwanji?( Moyo!! Moyo!!) Moyo unakhala bwanji?( Moyo!! Moyo!!)// Nanga tidzikhala bwanji?(tidzikhala bwanji??!!... Motherless) @Conqueror music group |
Sharing is cool
You may also like...
Mobile Site
Review
Comments
