Vote For This Song

Lyrics

(Intro) Yayayayayah Ya ya Yayayayayah Ya ya Ankati ineyo ndi mfana eh Mabodza chaka Chino nde ndichanga ineyo mumanama Yayayayayah Ankati ineyo ndi mfana Mabodza chaka Chino nde ndichanga ineyo mumanama Yayayayayah (Verse 1) Ndinablowa ndikubanda Koma ndimadana ndiza chamba Sine mfana wamumpanda But I got skills in abundance Mwina ndi zomwe ndimamangazi Kapena pasha ndimavalayi Kwa ine akazi ndima dalazi Kwa ine akazi ndima dalazi Yea kumenya ma hit back to back track on track Rapper kubwela kupanga attack attack Koma osamuyakha ine si size yake Pitani mukauzane simungamake (Hook) Ankati ineyo ndi mfana eh Mabodza chaka Chino nde ndichanga ineyo mumanama Yayayayayah Ankati ineyo ndi mfana Mabodza chaka Chino nde ndichanga ineyo mumanama Yayayayayah (Verse 2) See the DJ play my song at the bar I'm a star, understand I'm baba voss gimme props no jokes Don't you ever cross me inkosi yamakosi Call me Kris Kross, offwhite socks White airforce, sports car two doors I pay my bills no bankrupt Mr money ndili instant Ask your girls ndine merchant Mu new school ndine legend Since 2016 I've been rapping for my team 20-20 vision now I'm living my dream wusup (Hook) Ankati ineyo ndi mfana eh Mabodza chaka Chino nde ndichanga ineyo mumanama Yayayayayah Ankati ineyo ndi mfana Mabodza chaka Chino nde ndichanga ineyo mumanama Yayayayayah (Outro) Hahaha ayeh madness Yayayayayah Ya ya Yayayayayah Ya ya

Sharing is cool

You may also like...



Mobile Site

To view this page on the Malawi-Music.com mobile site Click here

Review

Comments
Hits 1196 Plays. | 33627 Downloads.

Follow Malawi Music on Instagram