Watch and Download Music Video



Download this video

Vote For This Song

Lyrics

Thila thila thila thila This is an awesome turn up song...And i so happen to have half the lyrics Verse 2(Donzo): Odi nkodze kaye Nsipe kaye nsilikali_ atino ndi shots on shots on shots on shots Nangaso tichite bwanji Mwati padheni ndipiturrr Coz am Mixing drinks and chips chicks kiss, spit, Spilt ma kids on her lips take pix, then take another piss Mwati kwamasteni ndzikaticha? Napalamulaso, akawonela maso , akakalipanso.. Koma ama_nso, ngati ali m'maso apa yalakwanso, Koma aaah Aka ndikachani, aka ka nkazi kandipatsa chiKhumbo aka, akandikachali alah! chemwa_li Ali Tiiwale mavuto ndati nzadziko, ngati malawi_ m'maona kuchedwa nde ma lawi tachita mwamachawi.. Saanakananso , she was a thirsty one nanga Ayi mayi Ananchita mwayi nanji n'nali nawo anayi ; mabotooolo Nantengana m'mafuna nkany*ng@na naye kenaka ndintaye coz she was digging me Mafosholo Ndayamba kulankhula chizungu, Chizungulile, chizungulileni kuseleku chisungunulileni Chikoke yani, chikokeleni chi mkazichi nchayani chayamba chizunguzime pukupuku matukutuku Kuzunguzuurrr Thukuta, ndachigunditsa kuchipupa chedwela pati kuputurr Zili pakamwazo Sitikamwaso_ ndayaka ndayaka ndayaka!! Kandulo! Ndampatsa mapasa pa mphasa pansi patebulo! sin'gona lero, Opposite ya sober lero Oooh! X2

Sharing is cool

You may also like...



Mobile Site

To view this page on the Malawi-Music.com mobile site Click here

Review

Comments
Hits 25532 Plays. | 23735 Downloads.

Follow Malawi Music on Instagram