Vote For This Song
Lyrics
Chorus Anyamata amasiku ano zibwana Dzibwana eeee dzibwana ( too much Children) Anyamata amasiku ano dzibwana Anyamata amasiku ano dzibwana Dzibwana eeee dzibwana ( you not grow up doing things like children all times) Anyamata amasiku ano dzibwana Verse 0ne Amayi akuti steniAbambo akuti m’dala Dzibwana eee dzibwanaaaaaa Azakhali akuti mtizi Amalume akuti mkozi Dzibwana izi nzibwana zovala akuti swaga Ena mkumati ung’ono ung’ono Dzibwana eee nzibwana iiii Chorus Verse TwoAkumayenda matako pamtundaKumati aoneratu lil wayneiiiii Ife tikadzudzula akuti mtradi Sitayilo yometa akuti mohoku Kuyimba nyimboku akuti kumanza sound Akafuna kuyankhula ndimakolo Aaa big maninso trogi mwandishopherayi Ndiye sikundiwaza olo mpang’ono Zimataxi chonchi ngati matrogi ovala atumiki Timafunan ung’ono ung’ono wina wake waboo ma flat
|
Sharing is cool
You may also like...
Mobile Site
Review
Comments

Zibwana Songs | Wake Up Malawi » |