Vote For This Song
Lyrics
intro Step up recordz!! (Dzuka Malawi dzuka) uuuuu aaaa eeeh (Dzuka Malawi dzuka) uuuuu aaaa Chorus Malawi the warm heart of Africa ooooh yeeee X2Wake up Malawi Wake up Malawi eyaaa Wake up Malawi uuuu Wake up Malawi oooh Verse one Dziko lathu olitukula si president ayiiiKoma machitidwe athu ndi omwe akuononga dzikoli iii mmm Katangale ,dyera, kudzikundikira chuma eyiii Moyo odalira osafuna kulimbikiraaa ooowoo Dziko litukuka bwanji ngati athu akungosewera bawo? mmm Dziko litukuka bwanj ngati anthu akungodalira kulandira? eee Ayeeee eeee wake up Malawi mmm Ayeeee eeee wake up Malaaaaa wi iii Chorus Bridge (Dzuka Malawi dzuka) x2Mmmmmm mmmmm Verse two Tili nawo anthu andalama zankhani nkhanii ii oooohOmwe atha kukwanitsa kutsegula ma business ii iiii Ena mkupatako ntchito, Kwinaku nawo akukatamuka Koma ayi safuna ndalama zawo n’zamanyado basiii iii yeee Achinyamata kumasauka zochita akuzionaaaa eee Ati zochosa swaggie, sangachite kuopa kunyozeka kwa ma babie Zitheka bwanji dziko kukhala wathu ndalama wa amwenye? aaaaa Wake up Malawi uuuu Wake up Malawi Dziko lathu silosauka osauka ndimaganizidwe awanthu Dziko lathu silaumphawi awumphawi ndimaganizidwe awanthu Wake up Malawi choncho Wake up Malawi yeaah Wake up Malawi Wake up Malawi yeee Chorus
|
Songwriters
Don FoxxySharing is cool
You may also like...
Mobile Site
Review
The talented Don Foxxy takes time out to wake the country with this well composed tune. Enjoy!
Comments
8256 Plays. | 3276 Downloads.
« Zibwana | Zibwana Songs | Ndine Okonzeka » |