Vote For This Song
Lyrics
Intro Yaka yaka yoo Life life yandipatsa nyimbo Life Verse 1 Akanakhala amaonda ndikunenedwa Bwenzi ntatsala fupa ndikuvala thewera Anthu ali ndi nsambi Kunja kuno Pena ukamva nkhani yako, kulephera kudya kumene Ataikazingira, kuithira anyeziii Kuifaka kamchereee, ikumvekera bwino Iwe kulephera kulongosola, Kuzibakila Ulipo wekhaa, chigulu chachiluka Chorus Mbuye mbuye mukhale nane Daily daily daily aaah Dziko lindimeza ilii mmh Kamoyoka kasungeni Daily daily daily aah Akuopsa ndimunthu lero Kuposa nkhwere Mbuye muyende nane Daily daily daily aahh Daily daily daily daily daily daily ambuye Kamoyoka kasungeni Daily daily daily aahh Anawa inee ooh oooh Verse 2 Ndimatha kuona chipiringu mtatseka maaaso Ambiri ofuna kuona zoona mchawa wapitadi Ndimatha kuona momwe nkhuku zikukhwasuliiidwa Kunyadira kupita kwanga coz they were under pressure Pamaso kukusekelera Kumbali ndiwe laughing stock Pamaso kukusekelera kumbali ndiwe laughing stock Apa mpomwe umadziwa blood thicker than water Thank you my darling, Thank you my family There’s no turning back we here to stayyy Tricky, am feeling am feeling am feeling this beat yeah Chorus Mbuye muyende nanee Daily daily dily daily Dziko lindimeza ili ili ili Kamoyoka kasungeni Daily daily daily aaah Akuopsa ndimunthu lero, kuposa njoooka Mbuye mukhale nanee Daily daily daily daily Oh Nono Oh Nono Oh Nono Oh Nono Oh Nono Kamoyo kasungeni Daily daily daily aaaah Kasungeni daily daily daily Kasungeni daily daily daily |
Sharing is cool
You may also like...
Mobile Site
Review
Comments
