Vote For This Song
Lyrics
Ndi wabwino Yesu ndi wabwino Ndi wabwino Yesu ndi wabwino Ndi wabwino anzanga ndi wabwino Ndi wabwino Yesu ndi wabwino Pakuti onse anachimwa napelewera pamaso pa Yehova Panalibe njira ina Koma nsembe imene oyenera anali Yesu yekha Mwana wa M’lungu osalakwa Kudzafera machimo a iwe ndine m’bale Kuti tikhale nawo moyo Wosatha, lelo tikutchedwa ana a Yesu Christu wa moyo Lelo ndi kunthawi zonse... Ndi wabwino Yesu ndi wabwino Ndi wabwino Yesu ndi wabwino Ndi wabwino anzanga ndi wabwino Ndi wabwino Yesu ndi wabwino Dziko la Malawi, limene sitinasankhe kubadwiramo Koma munatidziwa tisanabadwe munatilenga modabwitsa Ndife odala Kukhala ndi moyo ndi chisomo Kupezeka m’tsiku la lero Abale anansi abwino Mulungu mumatikondera Chikonzero chanu chabwino Ndichopambana Ndi wabwino Yesu ndi wabwino Ndi wabwino Yesu ndi wabwino Ndi wabwino anzanga ndi wabwino Ndi wabwino Yesu ndi wabwino |
Sharing is cool
You may also like...
Mobile Site
Review
Comments
