Vote For This Song
Lyrics
CHANGES (NYASALAND version) LYRICS by Fredokiss nyasaland aise......nde amati ndi kumpanjetu.....eh! Malawi…..achina fredo aise! VERSE 1 ZINTHU ZAKE ZINGOKHALA CHIMODZIMODZI AISE/ GWIRA NTCHITO ZAKA ZAKA OSASINTHA AISE/ ATI AKWEZA MALIPIRO SIZIKUSINTHA AISE/ MWINA MWAKE, TIMAFELA KUKHULUPIRIKA/ MAFANA AUVAYA GELE KOMA NTCHITO OSAPEZEKA/ ZAKA ZAKA MAKOLO FEES ANAPELEKA/ MA DEGREE, DIPLOMA, AUTHELA NDENI/ NTCHITO ZAKE AUPASANASO PACHIWENIWENI/ SAAKUPATSA NTAJI OLO UFUNE KUPANGA GENI/ NDIPANGA BWANJI MFANA NDIFUNA NSAMALE STENI/ MFANA WALEMBA ENTRY ANSIYA MBWENUMBWENU/ ZONSE ZINGOFUNIKA MAFANA OZIWIKA/ FUNIKA WINAWAKE AKHALIRE KUMPHIKA/ APO BII! ATI ZONSE SIZICHITIKA/ UMPHAWI WATHU WAFIKA PO PATSILATU STICKER/ UMPHAWI WAMUGHETTO WAFIKATU POSATSIKA/ MAFANA AUBIZIKA BIZIKA MANGOMENYA BANDI MALUZI ANDIGWIRA NANGA NTANI MPATSE SAA-CHET/ ULULU WACHULUKA U KNOW I GATA CRUSH EEET/ ATI PA RADIO AUKAMBIRANA BU-DGEET/
HOOK
VERSE 2 ZOMWE ZIMACHITIKA ZIMAVUTA KUMVETSA/ UYO ANALI NZANGA KOMA AUFUNA KUNDIGWETSA/ UYO ANALI NDANI KOMA AUFUNA KUNDI KWEZA/ MBEWU ZA NDIMA NDIZOMWETU TIKUFETSA/ BOMA SILI SINTHA AMANGOSINTHA NDI MABEDWE/ ALENJE NDI OMWE AJA ANGO, SINTHA MA PHEDWE/ NKHANI NDIYOMWEIJA YANGOSINTHA MA MVEDWE/ DOLLAR NDI YOMWEIJA YANGOSINTHA MA GWEDWE/ NDALA INALI LOVA PA DENI ETI INKANGOSHALA/ INAPEZA VEPI, PANOPA IMANGOYAKA/ IMANGOYAKA NDI AZIMAYI IMANGO PLAKA/ SIIMAGULA PHWANYA PA DENI IFE SIITIKRAKA/ MA SISTEZ NAWO PANO, AKUTAKATA/ ATI MAFANAFE ATI NDI TSOGOLO LAMAWA/ ZIMAWASANGALATSA TIKATONYOKA NDI BAWA/ UYO ANALI MUNTHU PANO MATENDA AMANGO GAWA/ NDI TIYANA TOMWE PANO MATENDA AMANGO GAWA/ NDI MALUZI AMU GHETTO DOLLAR AMANGOGAWA/ UMOYO WAMU GHETTO PANO AKUNGOKAWA/ KANTSIKANAKA LERO, NZAKEYONSO MAWA/
HOOK
VERSE 3 PA DENI DOLLAR NJE MWINA BRAZ ILOWE JONI/ TINASONKHASONKHA KUTI BRAZ ILOWE JONI/ STENI NGONGOLENGONGOLE BRAZ ILOWE JONI/ 2I JULLY IFE TINAMVERA STENI/ BRAZ, SISTEZ, TONSE KUMVERA STEN/ MZUZU ZIPOLOWE NDE TINANGOSHALA NDENI/ THE WHOLE DAY, IFE TINASHALATU NDENI/ BRAZ IUVAYA JONI NDE IFE TISASOKONEZE/ BRAZ IFUNA IVAYE PAJNA IFIKE PA MPOPE/ NDENI MADZI NJE NDE TUUFUNA PA MPOPE/ KOMA PANJA PALIPONSE PALI ZIPOLOWE/ BRAZ IUFUNA IKAFIKETU IKAFIKE PAMPOPE/ APOLISI NAWO PANJA ALI PONSE PONSE/ BRAZ NAYO INANGOGOGOMA KUFIKA PAMPOPE/ INE NDILI PA WINDOW BRAZ ILI PA MPOPE/ RATATATATA BRAZ AISE.....AH! HOOK
ACHINA FREDO ADA......... ACHINA FREDO ASIE......... |
Songwriters
FredokissSharing is cool
You may also like...
Mobile Site
Review
Fredokiss never disappoints and he delivers yet again as he resurrects the classic "Changes" by Tupac. This is the Nyasaland version. Achina Fredo Aise!!!

« 2014 Mr Politician with Ace Dirty ft Edgar & Davis | Singles Songs | Adane Nane ft Ace Dirty » |