Vote For This Song
Lyrics
VERSE 1 Ndati ndikuwuze love yanga ndiyolimba Utha kundikana siku lina udzasimba Tangondilora uchilawe cha bad man Tapanga zotheka usachuluse makani mayi Ndikulonjeza ine sinzakudabula Chikondi ndilinacho chinazaza chitambula Just give me the keys let me enter in your heart Singavayire wina you my number one chart Chimene ndikufuna nkazi undimveke mphete Ndikutengele pena ma hater akhale chete Daily ndikavayira umagwanda ngati chakwamba Tandipase mita love yanga ndiyosayamba I can be that guy kanyamata kosamba Tachiyese wekha ndisachuluse zokamba I can be that guy kanyamata kosamba tachiyese wekha ndisachuluse zokamba CHORUS Pano utha kumandikana kanekane! Chifukwa sumandiziwaaa Utha kumayelekedwa Yelekwede! Chifukwa sumandifiraaa Koma ukazangondilora Udzasimba iweeee *2 Koma ukazangondiziwa Udzasimba iwee*2 Zachikondi cha ineee!! VERSE2 Zoti ndimakukhumba bwino bwino umayada Koma ndikavayira nanga bwanji umanyada Iwe tandilore suzapangaso regret Love yanga ndiyambiri ndikugayira chi plate Tizakhala limozi kulikose tizayenda No sonye koma kwacha tizasipenda Nanga bwanji umafuna nzikunyengelera Kapena umafuna kuti ndizikupemphelera Koma nkazi tasegula chikhomo Sendela pafupi tandipaseko milomo Be my main chick wanna take you to jameka Chilichose ndikwanisa tangopanga zotheka Zachikondi changa palipose fusafusa Ngati maliro mlaka umandidusadusa Zachikondi changa palipose fusafusa Ngati maliro mlaka umandidusadusa CHORUS BACK PRE-VERSE nanga bwanji umapwetekesatekesa ngati pachilonda Nanga nzanenenene bwanji zoti ndimakukonda Umangophwekesa phwekesa Umangochepesachepesa Ngati udzalesesalesesa zachikondi cha ineee!! |
Songwriters
Gaspa & SaintSharing is cool
You may also like...
Mobile Site
Review
Comments
