Vote For This Song

Lyrics

(Intro by Thews P) Mmmm hustle gang Ndi one Aaaaa Mmmmmm (Hook) Bwanji iwe umakanayi Kuti mkaziyu siwako iwe! Nanga iwe umakana yi Kuti sunapeleke mimba iwe! bwanji iwe umakana yi Kuti mkaziyu siwako uyu! Pano ndiye ukukana Ukuti mwanayi siwako! (Verse 1 by Benja) Dzana lija man munazitenga ngati shasha Mutafunsidwa za mimba mutaikana Lero lino bhasi nkhani yaphulika yokha Zadziwika ndinu mimba mwanayu munamupasa Mhh,,ndimwanayu mukufanana Nanga bwanji mukumkana apayi? Mukalimbika kukanaku Ndisaname man ine pano ndikukhapani! Mmmmm (Hook) (Verse 2 by Thews P) Umangotinamiza kuti ulibe wina yi Koma kumbali ukupanga zina ndi zinayi makolo ake pano nde akuvutisayi Akunena kuti ndiwe amene wamutupisayi Kodi khalidwe lako ndilotani Umangofuna kumuonongera ma plan Bwenzi iyeyo atapangatu zina Anthu pano Akanamutchatu makhumutcha Mmmmh (Hook) (Verse 3 by King g) Bwanji umakana kuti mkaziyu siwako! Koma mtima kuzunza Mtima kuzunza Man mulibe chilungamo Chabwino ndakumvesa kuti kaziyu siwako Koma tawona mfanayu Chipumi ukufanana Taona mfanayu matewe ukufanana Koma sizitheka kuti mkaziyu umusiye!

Sharing is cool

You may also like...



Mobile Site

To view this page on the Malawi-Music.com mobile site Click here

Review

Comments
Hits 3953 Plays. | 1263 Downloads.
Singles Songs Amazitcha Makhumutcha »

Follow Malawi Music on Instagram