Vote For This Song
Lyrics
Intro B city L city B city x6Murphy chibwana! heptik,mwanache! Oh yeah! oh yeah yeaaaah guttah! Chorus Uzadziwa bwanji? We represent MdubzWe kip it turnup! Turnup! Uzaziwa bwanji? Malawi on fire! We kip it blazed up blazed up Black red green from the motherland & sititaya chikhalidwe each & every city now we murder dem all loard have mercy yaaaaaa oooh loard have mercy yaaa Verse 1: Heptik Bcity was a city of dreams kale kalekuli Young kay incyt ndi azinzake pano kwangochuluka timafana tongofuna chizungu sichingalamule dziko la akuda/tiphwanya chitaganya ngati nthawi yasamunda mukupha btwn guyz guyz simukutha life ya mu video kumalawi ya shupha u think ur classic new school rap it aint preaty copying style from lemmar it aint sick yaaa ndi bwelele mu chichew ndine oopya ngati Aidz uzindipewa ndife mitunda inu miseseleka kuimba mukuimba koma guyz sizikumveka afana a international olo pa channel sapezeka nyimbozanuzi mwina amamvela ma neighbour omvela nyimbo zako axse ndiochepa Chorus Verse 2: Mwanache Chamba chimene chitu chimadananchamba muzapenga ndinu mafana kodi ndiliti munayamba mukumangonamizana mukamamenya ma free style koma mumazimvera nokha zimene mumakamba mmafuna ukhala ngati akunja ngati akunja amakuziwani nkomwe aaa inu tasinthani nkoni ati kubwera ka call tone nso yakunja zanu nanga bwanji aaah inu tasinthani tone choti mudziwe nchoti you can never be them try competetion maybe u can try to reach them komano zomakopela sopano muzingotaya nthawi nyengo yake sipano kuno ndikumala kuno siku UK zimene mukukamba zivuta kuti ndikhululuke kodi baxi mmaona ngati nku america kulibwino muziimbanso ngati evans mereka Bridge: Murphy Zaozo zongo copera anawa "mbola"/ Saziwa komwe akulowera anawa so "blind" /anawa ndimabombo crat ona angosocheraaaaaChorus |
Songwriters
Heptik, Mwanache, Murphy, Janta, TrickySharing is cool
You may also like...
Mobile Site
Review
Comments
