Watch and Download Music Video



Download this video

Vote For This Song

Lyrics

Verse 1 (IKK) Kodi ndiwe ndani lako dzina/ Tiye pa Dance floor pang’ono Tingovina/ Chilichonse ukufuna panopa uzimwa/ Munthu olungama pa iwe atha kuchimwa Thupi lako, mbina yako zili nyatwa Opanda Dora pa iwe sanga peze mpata Mtima wanga pa iwe wangomata Ine njale iweyo yanga starter Uli steel ngati mac siuzatha Ndiwe Ndiku Diwa pano Ndikuthatha Information ya Dora Zanga uzisunga Data Kubwera kwako mumtima mwanga muli bata Kulikonse pa mbuyo ndizikusata Osasiyana nawe ngati thabwa ndi lata Auze makape pano uli m’manja mwa shata Osati Rasta ndati shata Hook (BUCCI) Babe thupi lakolo fire! Kankhope kako fire! Wabukisa moto fire! Ndakakanika kuzimitsa owo oooH! Ndipanga za iwe basi fire to fire Iwe! Fire to fire*2 Ndipanga za iwe basi moto ku moto Iwe! Moto ku moto*2 Verse 2 (BUCCI) Oooh girl you got my attention Somethinh I can turn away from Look how you got my heart… my heart brazing, burning fire fire Ndanjenjemera wandipasa ma filu ine phuma uuuuuuuuuuuuuuu! Wamatilira game ndiyako wamangilira Palibe omaka palibe omaka No ooo ooo aaa Wamangilira game ndiyako wamatilira palibe omaka paaa liiiiiiiibeeee…………… Hook (BUCCI) Verse 3 (IKK) Kodi kwanu mkuti Ndaombera kare ndiwe mufti Alipo kale kapena uli wekha Change banja ndiwe sindidekha Kungomwetulira paden ndikutenga Dora number one ndiwe ndapenga Iweyo first hustle yanga izibwera second Kuti timange banja tasala ndima seconds Ndukaikanso ngati uli ndi matenda M’mene ulili mwaiwe sangalowe matenda Owatumizayo Back to sender Ndikuphunitsa fast poti ndiwe Bomba Iwe siogwidwa ndima celeb ake ma zoba Ungolenga misala zomba Ukakakhala munyanja bwezi uli uyo Dora, yakoma, yosowa nsomba Hook (BUCCI)

Sharing is cool

You may also like...



Mobile Site

To view this page on the Malawi-Music.com mobile site Click here

Review

Comments
Hits 11601 Plays. | 4510 Downloads.
« Zoona Zanga (Feat. Zeze) IKK Music Songs Ndineshasha Ase ft Genius, Dan B, Blak Mamba and Muss (Prod By Dan B) »

Follow Malawi Music on Instagram