Vote For This Song
Lyrics
One of a kind Zakazi ena baby I'm so blind So hard to find Kukula nawe ndithu I wouldn't mind Umandiwaza Zochitika zako nzofasaaaa Mkazi wanga yi Ndithu CHAUTA uyu anapanga Beautiful woman Pa iweyo ndingasinthe chani Mkazi wowala ndi mtima momwe Ndimubise bwanji Beautiful woman Pa iweyo ndingasinthe chani Mkazi wowala ndi mtima momwe Ndimubise bwanji Ima Kaye eh Kaye eh Mpheteyi uyivale eh Vale eya Ima Kaye eh Kaye eh bwera ndikumale eh Male eya Funsa asisi Ndili nchikondi chozaza peace Kumva kukoma ndili pa ease Bwera pafupi nkupatse kiss mwaa Funsa a chimwene Ndikumayenda nditazazidwa ndi chimwemwe Nyengo ya Mvula wayisundasusa chilimwe Nde mundilole kuti leroli ndisimbwe eh Beautiful woman Pa iweyo ndingasinthe chani Mkazi wowala ndi mtima momwe Ndimubise bwanji Beautiful woman Pa iweyo ndingasinthe chani Mkazi wowala ndi mtima momwe Ndimubise bwanji Ima Kaye eh Kaye eh Mphete uyivale eh Vale eya Ima Kaye eh Kaye eh bwera ndikumale eh Male eya |
Sharing is cool
You may also like...
Mobile Site
Review
Comments
