Vote For This Song
Lyrics
TTT tElLeM Yahman yah Yah yah yah JahJah amakonda tonse Kuchoka mu nthawi ya Mose Ndipake anatuma nkhoswe Itiyang'anile izatisogoze Komabe sitingakhonze zonse Ubwino sitili nawo onse Timapasidwa mwayi oti tikonze Pomwe sifikila amayika Po step Mulungu wathu ndi wamphavu Wachifundo ndi Wa love Olo tigone osadya Iye amatizutsa kukacha Mulungu wathu ndi wamphavu Wachifundo ndi Wa love Olo tigone osadya Iye amatizutsa kukacha Eh eh eh Eh eh eh mhuu Mbuye Ali nafe amakonda Tonse Eh eh eh Eh eh eh mhuu Mavuto Ndiwo apanga munthu Sangaphe Zatsogolo lathu Poti chimwemwe ndi mtendere ndi zathu Ndeno woyipayo sangapangepo kanthu So one love is the language I chose I'd care about the others if I was in their shoes Kumasunga mangawa supindula kanthu Ungozizunza wekha pokonda milandu Mulungu wathu ndi wamphavu Wachifundo ndi Wa love Olo tigone osadya Iye amatizutsa kukacha Mulungu wathu ndi wamphavu Wachifundo ndi Wa love Olo tigone osadya Iye amatizutsa kukacha Eh eh eh Eh eh eh mhuu Mbuye Ali nafe amakonda Tonse Eh eh eh Eh eh eh mhuu Mbuye all nafe amakonda tonse Konda tonse eh Konda tonse eh mhuu Konda TOnse eh Konda Tonse eh Mhuu mhuu mhuu Mulungu wathu ndi wamphavu Wachifundo ndi Wa love Olo tigone osadya Iye amatizutsa kukacha Mulungu wathu ndi wamphavu Wachifundo ndi Wa love Olo tigone osadya Iye amatizutsa kukacha Eh eh eh Eh eh eh mhuu Mbuye Ali nafe amakonda Tonse Eh eh eh Eh eh eh mhuu Mbuye Ali nafe amakonda TOnse |
Sharing is cool
You may also like...
Mobile Site
Review
Comments
