Vote For This Song
Lyrics
VERSE Anabadwa mwana wokongolaAkamayenda panseu amuna cheucheu Zochitika zake ndiza changu Safuna kuvutikila kanthu Makolo ake akudandaula kunyumba Sukulu yake anasiyila panjira Iye kwake nkuyenda yenda mumabala Akuzisaka zambili zamandede CHORUS Amakonda zamanded iyeyoAmafuna zamanyado iyeyo Usalimbane naye ameneyo musiye Amafuna zamanyado iyeyo VERSE Ndimatiliyo yenini yinela banjaAmuna amagwada kufunsila banja Mpaka ena amapeleka malowolo Koma iyeyo amangoti ine toto Safuna amuna olila Safuna amuna ochedwa Iye afuna amuna opata Alinazo zambili zamandede CHORUS Amakonda zamanded iyeyoAmafuna zamanyado iyeyo Usachedwe naye ameneyo iwe musiye Amafuna zamanyado iyeyo |
Sharing is cool
You may also like...
Mobile Site
Review
Comments

Zamanyado Songs | Patsogolo » |