Watch and Download Music Video



Download this video

Vote For This Song

Lyrics

virse 1 Hun Pomwe Mwakhalapa pompa apa / Analipo Ena Anka Dzipopa Apa / Ankandiuza Sadzandisiya / Ankati Ndine ndekha amafila / Eh Nawonso Anka Lonjeza / Kuti Sadza Longedza / Anasintha Mawanga / Kundiswera Mtima wanga Pre - Hook Anandipekera Dzinkhani / Kundionongera plan / Ndeno Undiudza Chani ? / Pereka Manifesto / Hook Kodi Suli Ngati Enawa? / Suli Ngati Enawa? / Sudzandi Thawa Chikondi Chikukoma baybay. . X2 Virse 2 Nde Nde Nde, Zimene mukunena / Anandiuzaponso Ena / No me No Life / No me No life / Pano Alimoyo / Anawa namiza awo..Anasintha Mawanga / Kundiswera Mtima wanga Back to Pre - Hook Back to Hook Bridge Ndifuna Kudziwa / Ngati Chikondi Chako Chimapanga Expire / Ndati Undiuze Iweo / Suzanditaya? Ndili Ndi Mantha Ineyo / Ndi Mantha Ineyo / Sindizadzipha Ineyo? .. Nanana

Songwriters

Jay Jay Cee

Sharing is cool

You may also like...



Mobile Site

To view this page on the Malawi-Music.com mobile site Click here

Review

Comments
Hits 87204 Plays. | 75105 Downloads.

Follow Malawi Music on Instagram