Watch and Download Music Video



Download this video

Vote For This Song

Lyrics

MACHESI LYRICS VERSE 1 Geli ndinamaliza timapepala ndili nato/ Inde school siimatha koma tilipobe tingapo/ Toti nkanati ndili ku dziko lina lakutali/ Tikanagwira ntchito koma osati ku Malawi/ Mdala vep inaima, ndi steniso divorce/ Pano anabalalika sitimashala limodzi/ Its been a couple of years now since I heard his voice/ Ndango-ganiza zongoiwala ndilibe choice/ My life is on fire, palibe ondiphula/ Singagweso mchikondi akazi aku Malawi anadula/ Ghetto yut alibe kwacha, akazi amamuthawa/ Akasangalala ndekuti wamwa ka bawa/ Chifukwa chomwe navaira ku geli sinduchiona/ Ndipanga bwanji inspire ana omwe akundiona/ Nde after kuboweka, ndinapanga chisankho/ Pano ndimangoyaka poti dziko ndila tsankho/ BRIDGE Nde zikangopezeka zi dollar, ndimangoganiza zongoyaka ngati machesi/ Kundipeza ku den kwathu mbola, bola komwe fanz ikuyaka ngati machesi/ CHORUS Utha kundiyatsira mogo ndine machesi/ Utha kundiyatsira m`bongo ndine machesi/ Ukandipeza ku nkalabongo ndine machesi/ Mechesi, machesi, machesi VERSE 2 Kukhala ku Malawi, ndikulimba mtima / Kuli anthu ikutha week osaona mbamu ya nsima/ Sindili pa ufulu ngati nthumba mulibe dollar/ Dollar za msonkho wanga wina chikwama anachitora/ Regimes do change but, things dont change / Ndimakhala ozizidwa ndi nkhanizi ngati sangie/ Am 25 I should `ve been driving my own range - rover/ I got papers koma ndine lova/ Pepani atsikana lero mbina sizisuntha/ Ndiimbe zoti mukamva ubongo wanu ukhuta/ chifukwa cha umphwawi akazi analowa mbola / utha kulandidwa lero dzulo utapheya lobola/ zimachitikazi zimandizunguza bongo/ mkona nkhawa zanga zimathera ku nkalabongo/ mfana wa degree, akungomwa nkalabongo/ after 2 years wa degree wadiwa ndi nkalabongo BRIDGE Nde zikangopezeka zi dollar, ndimangoganiza zongoyaka ngati machesi/ Kundipeza ku den kwathu mbola, bola komwe fanz ikuyaka ngati machesi/ CHORUS Utha kundiyatsira mogo ndine machesi/ Utha kundiyatsira m`bongo ndine machesi/ Ukandipeza ku nkalabongo ndine machesi/ Mechesi, machesi, machesi

Sharing is cool

You may also like...



Mobile Site

To view this page on the Malawi-Music.com mobile site Click here

Review

Comments
Hits 15676 Plays. | 7158 Downloads.

Follow Malawi Music on Instagram