Vote For This Song
Lyrics
HOOK!! Pa Malawi yavuta ndi ndalama basi Panopa yavuta ndindalama basi Ndikuti ndindalama basi Basi ndindalama basi! (X2) PRE CHORUS yavuta ndi ndalama basi Panopa ndi ndalama basi tikuti ndi ndalama basi Basi ndi ndalama basi VERSE 1 Pa Malawi yavuta ndi ndalama basi// Utha kuyenda kwambiri koma sungatole pansi// Kukwera bus kuona ntengo ndingosika basi// Kuonanso mtengo wamchere apa ndingokhala lansi// Kabaza njee bola kungoyenda pansi// Kugulanso nyama akuchulusa mafupa// Ine kuwafusa ati sorry mphwanga pepa// Kagule tomatoe akuti dhilu ndikutupa Miyambi imati time is money// Or ndizipeze man dollars ndi zimane// Olo nditakhala kuti ndilibe honey// Kugula bonya bolani andikwane// Amayi zikomo kwambiri munandilera//smunandipusise panopa ndinachenjera// Mikoko imati waulesiyo asadye//komatu olimbikafe dzuwa likulowa tisanadye// HOOK!! Pa Malawi yavuta ndi ndalama basi Panopa yavuta ndindalama basi Ndikuti ndindalama basi Basi ndindalama basi! (X2) PRE CHORUS yavuta ndi ndalama basi Panopa ndi ndalama basi tikuti ndi ndalama basi Basi ndi ndalama basi VERSE 2 Ndinali fulu anthu amandikamba// Ati ndinatha panopa sindikumasamba//chifukwa chamakala akuti ndine mlamba// Ndawauza yavuta ndi dola ya chakulamba// Chick kuti ikulole imafila zidola// Ati amafila mafana owala ngati solar// Akazi akumalawi panonso analowa dollar(yeah pano analowa mbola) Vuto lomwe lilipo kwa ex wanga Sarah// pamene ndilibe dola ati sindikumushala//ndapepha reback akuti ndizamisala// Ati ndimuleavy(ndimusiye)coz ndilibe kaisala// Ndeno ndinacrasher ndinathoka sten yanga// Ndinati panopa andivuta ndimafwalanga// Kufunsa ma boss ati dollar zikutalker// Ati popanda dollar pamalawi suutchu?kaaa// HOOK!! Pa Malawi yavuta ndi ndalama basi Panopa yavuta ndindalama basi Ndikuti ndindalama basi Basi ndindalama basi! (X2) PRE CHORUS yavuta ndi ndalama basi Panopa ndi ndalama basi tikuti ndi ndalama basi Basi ndi ndalama basi .... Chat Conversation End Type a message... |
Sharing is cool
You may also like...
Mobile Site
Review
Comments

Yavuta Ndi Ndalama (EP) Songs | Minyama ft Fewzy Rapper (Prod. HKP) » |