INTRO---ah king chambiecco....kamodzi kawili,,pachimkwezamau basi As alweys a.k.a zam'bongo ya know,,cyaa one to dem Uyu ndati nzamu kha kha,,kho kho,,khaaaa,,nzamugagada,,,phwaaaa,,uuuuuko,,aaaaaaha CHORUS-- akamabwera nzamuboboda,,(bobobo) Ndizibonga ndati nzamugogoda,,(gogogo) Uyu nzamukhapakhapa uyu,,(khakhakha) ndinkhwangwa uyu ndaona sinzanga uyu yes(*2) VERSE 1-- Azangodabwa kuti diiiiiiiiii,,,ndadina Cham'mbalimu azangomvera fiiiiii,,ndafinya Chanthitimu kuti ziiiiii,,ndazika N'nayenda ndisingano kaya ndaliza Chapaliombo kuti phwaaa,,,ndaphwanya Chanmusimu kuti Diiiiiii,,,ndaDina Osamusiya tsaya phwaaa,,ndaphwanya Thupi lonse kha khak haaa,,,ndagagada Ine ndati sinsekelera izi Kaya ngwankulu koma nzendewera izi Kaya n'yanzida ine sinlekelera izi Ah king chambiecco sinmweturilra izi
VERSE2-- Ndati nzamuchotsa chimbenene Nzamuliza nzamumvetsa manzenene Ngati nguli nzantulutsa manvenene Nzamuyamba kumutu m'paka chidendene yes(*2) Mpaka akanene kwa achimwene,,nenene Kuti ine n'ngwankali ine,,nenene Osalora zantudzu ine,,nenene Otamira legeni,,,ine ndemwene VERSE 3-- Yeeeeeeeeeees bad man afi run away,,athawe athawe Yeeeeeeeeees wamwanoyo nthana naye uko,,athawe athawe Athawe lantondo wadooka uko Akapezeka azondoooka uko Kamodzi kawiri ah king chambiecco A.K.A zam'bongo Kaya anthuwa amationa kuchepa masozi Kaya ndi ukanthitiwu,,koma ulendo uno tithana nawo Hooooooo ya ya ya ya ziliko kuno |