Vote For This Song
Lyrics
INTRO--pachimkwezamau basi,,, kamodzi kawili,,ah king chambiecco Kachikena,,abwere adona awo,,eeeiii,,eeeehe!!
CHORUS-- -pakamodzi Ubwere n'dzakuoneko -pakamodzi ubwere n'dzakukondeko -pakamodzi ubwere n'dzakugwireko -pakamodzi ubwere n'dzakupyontheko,,n'dzakuoneko,,n'dzakugwireko -Paka Paka Pa Pakamodzi --ubwere n'dzakugwireko --pakamodzi ubwere n'dzakukondeko --pakamodzi ubwere n'dzakuoneko --pakamodzi ubwere n'dzakupyontheko --pakamodzi ubwere n'dzakugwireko,,n'dzakuoneko --Paka Paka Pakamodzi
VERSE 1 -ndungofuna ntakuonako -ngungosowa ntendere ndikugonako -ubwere ufulumire n'dzakupyontheko,,n'dzakupapaseko,,n'dzakukondeko eeeei -timambama n'dzakumenyeko -zachikondi zosisita zokutsinako -kumashobi nkukutengako -nkuzagula zitumbuwa nkukumanako -kuzandithamangitsa iwe nkundigwirako -mwachikondi iweyo nkundifusako -daaaaarlin,,simundipatsako -hahahaha,,ine nkuzanyemako -zosewera zachikondi ka ubwanako -nchewa nkuzazimva ka ubwanako -kuzakugwira kukumbata nkundikanako -tchetera lachikondi nkuzasekako -kuzakukoka timasaya nkukudinako -choooooka!!!! Tima-Dimples timakhala chonchi iwe
(Back to chorus)
VERSE 2 -mubwere panyumba adona heeee -moyowu sukukoma ndekhandekha heeee -chilichonse chasiya kukoma heeee -ubwere ndidzadye zo_baker iweeee -zachikhathu zosapsa nkunonabeeee -kukanika kukalipa nkudekha ineeee --aaaaaaahaaaa!!!!!! -ndufuna ntakuona ineee -ndatopa ndekhandekha chiyenda yekha inee -ndazisowa zako zija zomeka weee -zovala zothina zosalalitsa iweee -weekend nyakula chilundu iweee -ine pakhonde manja nkhongo nsunamo nduu -kuganiza ndikuona liti mama weee -ukumandiimbitsa tinyimbo ya ya yeee!! -oooh na na na na na na na naah naah eeeeiiiiii -kamodzi kawili ah king chambiecco pachimkwezamau kaya zumvekaaa!! Mubwere adona inu
(Back to chorus then repeat verse one) |
Songwriters
King Chambiecco, Janta aka Jaxcy on The BeatSharing is cool
You may also like...
Mobile Site
Review
Pakamodzi by King Chambiecco. Produced by Janta
« Pasa Pasa Freestyle | Ndizamugogoda Songs | Get Down Low » |