Vote For This Song
Lyrics
Intro; Ine ndati sinsekelera izi, Sim'mwetulira ine izi Aaaaaha ! Kamodzi kawili katatu ! as always mokwezamau pachimkwezamau Ah king chambiecco, a.k.a zam'bongo Uthenga uli ndi ka ukali uwu koma mutimvetsese Yes !Real talk real talk I say Chorus Escom kuzangomenya black out again/ black out!Eti eti eti,eti black out again- pheeeeeing Water board nayo madzi asiya Akuti tichita bwanji ife awa, see dem go again Kuzangomenya black out again/black out! Eti eti eti,,Eti black out again- pheeeeeing Water board nayo madzi asiya Akuti tikhala bwanji ife awa, see dem go again Verse 1 Aaaaaaha!Amangothamanga kubwera kudzadula Mwezi wapita umodzi koma bill yakula Chifukwa chake nchani uuuuuuko!!!! Akuti zaDula Sanafotokoze nkomwe miter azula Eeehe Amangonamizira ku nkula awa Mesa zipangizo amati anagula awa Nanga bwanji zochita zawo sakukula awa Awa ndiye takwiya nawo kwambiri Back to Chorus Verse 2 EeeeeiMwezi watha koma madzi sakutuluka Zovala tungovala pano zungosuluka Thukuta kuchita kumata inu lisakutsukika Chuma kumapeleka koma sizusinthika Iiiiiiiiiiiiii Miyoyo yathu siikutukuka Chiopsezo chachuluka ubwino wapunguka Kuyera kungochepa,kuda kungochuluka Kamodzi kawili ah king chambiecco seh!!! Back to chorus x2 till end |
Songwriters
King Chambiecco, Snake JSharing is cool
You may also like...
Mobile Site
Review
Dancehall Artist, King Chambiecco has joined several voices blasting Blantyre Water Board and Escom for their incompetence in this new single. Chambiecco blasts Blantyre Water Bard for water outage and takes a swipe on state-owned power producing company, Escom for the blackouts.
Comments

Singles Songs | Gate Man » |