Watch and Download Music Video



Download this video

Vote For This Song

Lyrics

Intro Ya' already know what it is It's Kim Deezy Eazy Slapping these whack rappers With Punch after Punch one more time! Kudzuka mmawa kuyang'ana kwagwanji Palibe chagwa ndiye ndigwetsa punch Ndidzipange introduce kapena mumandiyada? Kupanga zaineyo ndeti mbiliyako yada Ndidzakusukuludza Ma hater alipo ambiri akudabwa siukuluza Pa beat ndima spinner TOYOTA cruiser OG salowelela zosamukhuza Musakanene bodza apatilitonse Ine sindiopa tima rapper tilitonse Amadzimva u Young king nde dikila tiatonse Kutchuka ndikwanu koma skill ndiyatonse! Game ndikumakana ndiyetsela ndimakako Kufuna kundisuntha ndeyetsela ndimakako Sikamadza kokha Ine ndiwakunyanja ntchito yanga ndimakoka Koma ndikasanja zima babe ndimakako Ndipo sindimafooka Pa top osachoka Ndakulandani joker inu ndi ana anjoka Beat yi ndi Diva ndimaikwelakwela Sikuyamba kuipha imandifelafela Ndikuyamba kundimva?uzindimvelamvela Ma babe amandifeela ngat tima aluvela Ndinakwatila beat ndimakhala ku stu ndukhala pachikamwini Ndinapachika nkhawa anadzipachika mwini Ngati mtengo Wa Gwafa pa beat ndimatelela Ineyo ndi machine ma truck ndi ma telela Uthakuona mmene nyimbozi ndimaphelela Mwina ndili ndidziwanda nde muzindipemphelera ndaoloka dzilumbazi Ndimaika rap osati lumbazi Kumveka Mangochi mpaka Lumbadzi HEYO GD yafika yaMijombazi Chaka chino ulaliki ndi anga ma verse Odziwa malemba ndiomwe angamamvese Koma ndilalikabe enawo abalalika Ndikayamba ineyo enawo abalalika Ena apakatika Ena atapatika Mafana ndimapweteka nkuwaudza zimachitika Mumachulutsa kudzithemba Kudzithembelela Ena mukapsa moto chifukwa mmadzithembelera Nawe Ace jizzy undibwenzere Yanga dollar Collabo yachaka chatha mpaka lero osayimba Kapena mutamvera munadziwa simulimba Hhaa? Kwachuluka ma guy amisomali Amatikhomelera Mkumatigonelera Sindidziwonelera nane ndovuta kulela Pa beat ndine wa umve nde mudzidwala kolela Sangakhale fly ndatenga chokolela Siulipo wekha mulipo kaphava Oimba oipa okuba mbava! vibe yako ili bho koma lyrical mbola Umayetsa uli ndi bomba koma lilikombola Ndimaika ma Punch umaika malido Iwe kuimba ndine ungakhale Nkhomaliro Tingasonkhane kwanu kungakhale maliro kundisata ineyo ukusata imfa Oyimba wazima tracksuit za taifa Siumavala zodhula Khosilo ndikudula Kukumenya kumuutu nkusakaniza medulla Anthu ngati inuyo chakunoko timabhula Zovala ndikuvula Kaujeni ndikudula Mulibwanji ma hater koma coffee mwamwa? Mafana owononga paliponse coffee mwamwaa! Ineyo sindinati koma apapa ndikukamwa Ati beat ndailuma ndikukamwa Ngakhale muli Ng'ombe sindikudya beef ndikukama Mumagona pa beat ife timagona pakama Mumabwera ndimatama kuzitama Ndimabwera ndimambama zimajudo kuchigama! Ndimabwera ndima PUNCH AFTER PUNCH AFTER PUNCH ?

Sharing is cool

You may also like...



Mobile Site

To view this page on the Malawi-Music.com mobile site Click here

Review

Comments
Hits 20 Plays. | 82 Downloads.

Follow Malawi Music on Instagram