Vote For This Song

Lyrics

ALI NDI ZAKA 31 NDALA YANGA INAMUUZA AMVEKELE…FISI NDI FISI!/ OLO ASINTHE THENGO ,AMAKHALABE FISI/ OLO MFANA WAKE AMAZAKHALABE FISI/ TINKANENA UJA LERO AUTHELA MU SIZI/ JZU ANATHOKA MULTIPARTY KNONDO/ YOPANDA MIKONDO/ KNHONDO YA MIZIMU YA MAGANIZIDWE NKHONDO YA UMPHAWI ETI UKO WANTCHITO WAWO AMAMVINILA/ AKAAMAAPHIKILA AMAMUVINILA/ AKAMAPAKULA, AMAMUVINIILA/ PAMAPETO AKE ETI AMAMULIPILA/ AM SWIMMING SO DEEP LET ME GO ALITTLE SHALOW/ NKHONDO YA MIPENI TUUVUNGA ZIBALOBALO/ MMBURUNDI KUTSEGULA OKALA ISANDUKA WHOLESALE/ MMALAWI KUTSEGULA WHOLE SALE ISANDUUKA OKALA/ AWO ANABA DOLLAR, TINAAVOTERABE/ UYU AKUBA LERO ,TIZAMUVOTERABE/ KUNJAKUTU KWACHA KOMA UKUTYOLERABE/ ANANSHUTA MPHWIYO NDANI?/ CHIFUKWA CHANI?/ GALIMOTO LA NJAUNJE ANAOTCHA NDANI?/ NOTHING IS IMPOSSIBLE/ YESU ANANDZUTSA LAZAROTU ATADIWA/ NSINGA ZA NKONONO PA IWEO ZAMANGIDWA/ JAH PATSOGOLO NSINGAZO ZIMASULIDWA/ JAH PATSOGOLO TIDZUTSANA MMODZI MMODZI DZUUKA!!!!

Sharing is cool

You may also like...



Mobile Site

To view this page on the Malawi-Music.com mobile site Click here

Review

Comments
Hits 76634 Plays. | 80874 Downloads.

Follow Malawi Music on Instagram