Vote For This Song
Lyrics
Verse 1 Unandipeza ndili lova Ndilibe kalikonse Mmatumba mwanga mobooka Nyumba yopanda khonde Ndekuti dzuwa likaomba Mkati khuma kumaonda Iweyo utandiona Sindimvetsa chomwe unakonda Utabwela unandilimbikitsa unati ndisabwelele m'mbuyo Chomwe chinali chako naneso ndi changa Kuti ndisamasowe tulo Bridge You must be a saint or something How could you give it all And ask for nothing in return Pre chorus Ndikusowa chonena ine Malangizo ako Andifikitsa pena ine Poti ndiine wako Hook Bwela umunyadile mamuna amene ndili Kamba ka iwe X2 Verse 2 For I was never enough I had room for you in my life Ndizizwa ndichisankho chako ooh Chokhala nane ngakhale mnyumba mwanga Mpando munalibe Pomwe sizinkandiyendela Unagwada ndikupemphela Pamene mwayi unatetela Unandiuza ndimukumbuke namalenga Ndikamabwela ku ulenje Mmalo mwa nyama ndi denje Nkumandilandilabe ndi chimwemwe Ine pakamwa kakasi You know pena ndikati ndidye frus Most of my days i am under the weather But i believe God gave you to me To help me keep it together Bridge You must be a saint or something How could you give it all And ask for nothing in return Pre hook Ndikusowa chonena ine Malangizo ako Andifikisa pena ine Poti ndine wako Hook Bwela umunyandile mamuna amene ndili Kamba ka iwee X4 ( chikondi ndachimvesesa// nkhawa zonse unathesa// chikondi ndachimvesesa I'm a better man// sindikanakwanitsa ndekha// i needed you to get me to where i am right now//) |
Sharing is cool
You may also like...
Mobile Site
Review
Comments
26160 Plays. | 66369 Downloads.