Vote For This Song
Lyrics
VERSE 1 Honey iwe zomwe wandimvetsa mtimamu ah inenenene ah inenenene eeh haa Honey iwe iiih ntima wako ndiotani iwe iweee ah inenenene ah inenenene Ngakhale nkhawa yaing'ono ako maso alunjike kwa ine ukusowa chani iwe ndiuze ndikakufikile pali iwe BRIDGE poti mwa anzanga onsewa mwa amuna onsewa palibe mamuna amene akumva ngati ine palibe palibe poti alibe alibe awa mphumi ngati ineyo poti ndinapata CHORUS Zonse mwa mmodzi X2 zonse zonse zonse zonse eyaa Zonse mwa mmodzi X2 zonse zonse zonse zonse eyaa ndi mmene ulili ndithudi ndangoyenela kukutenga uli ndi zonse zonse zonse zonse eyaaa X2 VERSE 2 ndikutali komwe tikulowela-lowela But knowing that ive got you by my side suddenly everything is simplified mumdima sinzayenda ndekha ine sungalore iwe kukawala sindingayende ndekha sindigalole ine zonse zomwe ndifuna you got it plus more!!! pa iwe ine liuma uuhh darling I know!!! BRIDGE poti mwa anzanga onsewa mwa amuna onsewa palibe mamuna amene akumva ngati ine palibe palibe poti alibe alibe awa mphumi ngati ineyo poti ndinapata CHORUS Zonse mwa mmodzi X2 zonse zonse zonse zonse eyaa Zonse mwa mmodzi X2 zonse zonse zonse zonse eyaa ndi mmene ulili ndithudi ndangoyenela kukutenga uli ndi zonse zonse zonse zonse eyaaa X2 BRIDGE 2 Umankonda ndani inee Ndimamukonda ndani iwe Nyimboyi ndi yandani iwe iwe iwe iwe iwe X3 CHORUS Zonse mwa mmodzi X2 zonse zonse zonse zonse eyaa Zonse mwa mmodzi X2 zonse zonse zonse zonse eyaa ndi mmene ulili ndithudi ndangoyenela kukutenga uli ndi zonse zonse zonse zonse eyaaa X2 |
Sharing is cool
You may also like...
Mobile Site
Review
Comments

« Access Granted (Prod. Blage) | Honest EP Songs | Kuyambira Lero (Prod. Dj Sley) » |