Vote For This Song
Lyrics
Intro (This is Stichfray production) Huh Koma lerolo (yeah) ndikubelani (aah) Ndikuuzani ine apa ndikubelani (Macholowe) Manyumba anuo mukangosiya osatseka bwinobwino (Macholowe) Chitetezo chosakwana (aah!) Ndikubelani ndikuuzani (Its your boy Mascot) Yemwe samadziwa za dzina langa ndani/ Yemwe samadziwa kuti ndimalanga ndani/ Okay n'kufunse chonchi bra/ Unaonako nyumba yopanda ma bagala ba/ Unaonako munthu osaopa akuba/ Ngakhale ku state house kumakhala khoba/ N'khale ma bankinso amaopa ma armed robber/ Tsono choncho wakuba mungamamutenge zoba/ Huh!!!! Hook Ndavala nkhwani nkhwani kunkhopeku ndavala mask/ Mmanja muli gun gun pakati pausiku kuhasa/ Ena amanditcha mbava ena kawalala/ Maina ngambirimbiri koma ndimakonda la Macholowe/ (Haaaaaaa!!!!) Macholowe/ Macholowe/ Macholowe/ Ndine Macholowe/ Macholowe ndine Macholowe/ Macholowe ndine Macholowe/ Manyumba anuo mukangosiya osatseka bwinobwino Chitetezo chosakwana Ndikubelani ndikuuzani hahaaaaa Komatu pena pake ndimakufunilani za bho/ Ndimakondwera mukakhala ndi dola nkuma baller/ Nanga ndingakubeleni bwanji mulibe kanthu/ Nanunso mutha kubwera kuzaba kwathu/ Ine si Zambian koma ndine wo'lusaka'/ Ndili ndichithumba nkona apolisi akundisaka/ Mawa ndizaba kwanu ukakhala ndi soka/ Ndidola zomwezo nkazi wako uja ndisoka/ Kugwidwa ndikoophya komabe sindiopa/ Business iliyonse ndi risk pena imaflopa/ Iliyonseyo ndi dilu bola ndipeze cholowa/ Ndakuuza kale phwanga ndine Macholowe/ Haaaaa!!! Hook Ndavala nkhwani nkhwani kunkhopeku ndavala mask/ Mmanja muli gun gun pakati pausiku kuhasa/ Ena amanditcha mbava ena kawalala/ Maina ngambirimbiri koma ndimakonda la Macholowe/ (Haaaaaaa!!!!) Macholowe/ Macholowe/ Macholowe/ Ndine Macholowe/ Macholowe ndine Macholowe/ Macholowe ndine Macholowe/ Bridge Palibe anasankha kuti basi ndikhale mbava/ Palibe angakondwe kuti adzishala lova/ Tidzifunse kuti chinamuyambitsa munthuyu ndichani/ Tisanamunyoze kumujaja kaya kumutani/ Palibe anasankha kuti basi ndikhale mbava/ Palibe angakondwe kuti adzishala lova/ Tidzifunse kuti chinamuyambitsa munthuyu ndichani/ Tisanamunyoze kumujaja kaya kumutani/ Hook Ndavala nkhwani nkhwani kunkhopeku ndavala mask/ Mmanja muli gun gun pakati pausiku kuhasa/ Ena amanditcha mbava ena kawalala/ Maina ngambirimbiri koma ndimakonda la Macholowe/ (Haaaaaaa!!!!) Macholowe/ Macholowe/ Macholowe/ Ndine Macholowe/ Macholowe ndine Macholowe/ Macholowe ndine Macholowe/ Ndavala nkhwani nkhwani kunkhopeku ndavala mask/ Mmanja muli gun gun pakati pausiku kuhasa/ Ena amanditcha mbava ena kawalala/ Maina ngambirimbiri koma ndimakonda la Macholowe/ (Haaaaaaa!!!!) Macholowe/ Macholowe/ Macholowe/ Ndine Macholowe/ Macholowe ndine Macholowe/ Macholowe ndine Macholowe/ Outro Ndikuuza ine apa ndikubelani |
Songwriters
MascotSharing is cool
You may also like...
Mobile Site
Review
Comments

G.L.C (Good Luck Charm) Mixtape Part 2 Songs | Kodi Bwanji (Prod by BFB and MBJ) » |