Vote For This Song

Lyrics

INTRO Aaaaah aaaaah aaaaaaaah!! De mitso 265, am a 265 Am a superstar Afriswami yeeeH!! VERSE 1 mafunyeta anagwa anthu amkati asthma/ Omwewo super star anazima/ Martse kuotcheka ndi moto/ tremor kugundidwa ndi galimoto/ Wary cris achalume/ Akanadwara tikanati akapume/ Koma onsewa ngozi/ Malawi wadzadza ndimagazi/ Chikuchitika ndichani kumpanje/ Kutentha kwathupi taluza nako atoti manje/ Grace chinga anapita mwachidule/ kutisiya zambiri asanaulure/ [kalangaaa!!!] CHORUS (Imfa ya super star yomvetsa chisoni ngat usatchuke)×2 Koma ndikaganizira Zima vibe luxury life ndiyera kutchukaaaa!!! VERSE 2 Imfa ya celeb / Sungayimvetsetse ngat sentence yopanga verb/ Imakhara yomvetsa chisoni/ Mafunso kuchuluka chachitika mchani/ Umva wagwa ndipo wamwalira / Fans yonse kusanduka anamalira/ Ine monga oyimba wa ng'ono/ Imfayi imandizizilitsa nkhongono/ Paliponse ululu/ Odandaula amakhala gulu/ Pompopompo ndimabweza gear/ Kupita ku studio ndimadza siya/ [ koma 2 Mina minaaaa!!!!!]

Sharing is cool

You may also like...



Mobile Site

To view this page on the Malawi-Music.com mobile site Click here

Review

Comments
Hits 251 Plays. | 177 Downloads.

Follow Malawi Music on Instagram