Vote For This Song
Lyrics
Intro Yeah, Look Verse 1 (Macelba) Unawina mtima wanga ndiwe boma/ Chikondi chakwela nde sitingatsutse boma/ Inu nde a chair kulamulira boma / Mamie muimanso silingaluze boma/ Mamie muli ndi mtima wachikondi / Olo ndilakwitse muli ndi mtima wachisoni/ Makutu m’natseka muli ndi mtima wachigonthi/ Siinu a njilu mulibe mtima wachizondi/ Ndinene tchutchutchu olo atsine khutu / Sindimva za munthu kapena ndi juju/ Mtima wanga za inu unachongelatu/ Ndabwera ndabwera apapa ndafikiratu/ Chorus (Saint) Mamie iwee ndasankha (no regret ) Mamie iwee ndasankha (there is no recount) oh wina basi no wina Palibeso wina ndiwe Owina Oh wina basi no wina Palibenso wina Ndiwe owina Verse 2 (LuLu) Nthawi yomwetulila nchimake/ Mtunda watha ngati owina uli ndi ine/ Mamie chonde chilemekeZe chikondi mammie/ Mumtima mwanga ndakudulila ka munda mammie/ Zili ndi iwe kulima tiligu ndizokondwela mammie/ Zili ndi iwe kulima nansongole ndizilila/ Chorus (Saint) Mamie iwee ndasankha (no regret ) Mamie iwee ndasankha (there is no recount) oh wina basi no wina Palibeso wina ndiwe Owina Oh wina basi no wina Palibenso wina Ndiwe owina Verse 3 (Macelba) Ndikamaseka umaseka nane / Ukamalira mtima umasweka nane/ Nazelezeka nawe wabaizika nane / Mmene umandikondera ndimakukonda nane/ Owina owina/ Wamuntima mwanga ndiwe no wina/ Owina owina/ wamuntima mwanga ndiwe no wina/ Chorus (Saint) Mamie iwee ndasankha (no regret ) Mamie iwee ndasankha (there is no recount) oh wina basi no wina Palibeso wina ndiwe Owina Oh wina basi no wina Palibenso wina Ndiwe owina |
Sharing is cool
You may also like...
Mobile Site
Review
Comments
