Vote For This Song

Lyrics

Intro Ooooh yeah…!!! Compare…!!!! Mr Ayaya aaah..!! Verse 1 Anakuyikako pa dp status yomawona wekha / Muchikondi ichi chi kalikose anthu akawona/ Nkhani yako sinakambidwepo pa mikozi/ Muchibwenzi ichi alemba/ Sanayambe wakumenyelako nyimbo/ Muchikondi ichi ndiyimba/ Undipatse potential ya pa easy love ya serious/ Mwachinsinsi mwachinunu opanda nazo violence/ Love yanga imaposa ma merchant/ Kuwala kubhebha rain ball paint/ Kwa zake samakutchula hunie/ Muchikondi ichi ndikwanitsa/ (HOOK) Umakonda competition Undipange compare (compe!!!) Love yanga ili pa msika Undipange compare (compe!!!) Undipange compare compare Ndichikondi cha enawa Undipange compare compare Ndichikondi cha enawa Am special am special babe!!!! Am special am special babe!!!! Verse 2 Unayamba wapitapo ku Nyanja/ Kapena kukutengera kunja/ Vama lavu ife ndakamuna/ Pa chikondi kuno nkuchikweza/ Ndimayatsa moto onyeketsa/ Chikondi chovuta kuzimitsa/ Ufike pomadzifusa ndineyo/ Akundikonda choncho iyeyo/ Anakugulirako bundle mofaya/ Gift ya pizza mofaya/ Mu love iyi uchongetsa/ Mu chikondi ichi ndikwanitsa/ (HOOK) Umakonda competition Undipange compare (compe!!!) Love yanga ili pa msika Undipange compare (compe!!!) Undipange compare compare Ndichikondi cha enawa Undipange compare compare Ndichikondi cha enawa Am special (mmmm….special) am special babe!!!! (mmmm...special) Am special am special babe!!!! Verse 3 Anayamba wakugulirako RVD/ Muchibwenzi ichi uvala/ Umachita kusowa kopita/ Iweo kusowa zochita/ Mu chikondi ichi chokha/ Ndikusamala ndikuchengetera/ Pa chikondi ichi chokha Sukubetsa ndikuteteza/ Ukazangondisiya hunie/ Uzangomva ine ndapenga/ Wandifo-wandifowola/ Pa chikondi ichi sindichoka/ (HOOK) Umakonda competition Undipange compare (compe!!!) Love yanga ili pa msika Undipange compare (compe!!!) Undipange compare compare Ndichikondi cha enawa Undipange compare compare Ndichikondi cha enawa (HOOK) Umakonda competition Undipange compare (compe!!!) Love yanga ili pa msika Undipange compare (compe!!!) Undipange compare compare Ndichikondi cha enawa Undipange compare compare Ndichikondi cha enawa

Sharing is cool

You may also like...



Mobile Site

To view this page on the Malawi-Music.com mobile site Click here

Review

Comments
Hits 480 Plays. | 313 Downloads.

Follow Malawi Music on Instagram