Vote For This Song
Lyrics
Verse 1Sinabwele kuzangodya kumapita Kumapita no Sinabwele kuzacheza kumapita Ine kumapita no Kapena kuzangowona kumapita Ine kumapita no Ndabwela kuzakhazikika moyo Mwako lady Chorus
Usakayike eee sine mlendo
Moyo mwako bady sindichoka eee
Usakayike eee sine mlendo ndikhazikika bady
Sindichoka oh oh oh oh oh
Verse 2
Sinabwele kuzapanga masewela
Masewela no
Kapena kuzakhumudwitsa mtima wako
Mtima wako oh no
Sindifuna kungodusa kumapita
Ine kumapita no
Ndabwela kuzakhazikika mdziko lako oh ooh
Verse 3
Uuuuu oh oh oh oh nesnes
Sinabwele kuzangodya kumapita
Kumapita no
Sinabwele kuzacheza kumapita
Ine kumapia no
Kapena kuzangowona kumapita
Ine kumapita no
Ndabwela kuzakhazikika moyo
Mwako lady
|
Songwriters
NesNes, Dj SleySharing is cool
You may also like...
Mobile Site
Review
NesNes links up with Maloto hitmaker, producer Dj Sley for this fresh new hit.
Comments
