Vote For This Song

Lyrics

Ndikonda zomwe ukonda Kodi wekha sudziwa Ndikonda kukhala pafupi nawe Suona chikondi mmaso mwanga Ndikonda kuchita zonse undiuza Zonse unena nthudi ndichita Ndikupepesa pa zonse zomwe ndinachita Ndikupepesa pa zonse zomwe nakulakwiira Ndikupepesa pokunamiza kuswa mtima wako Ndikupepesa pokhala mkazi yemwe sunafune Ndipanga chilichose kut ndiloweso mmalo Ndipanga chilichose Kuti ndiloweso malo Chikond chako nnaseweretsa U opened the door yes I did shut it Ndmkaonangat am e clever one Leaving u like that Leaving u stranded koma ndazindikiraa Aaaaaa Ndazindikira aaaaaa Aaaaaaaa aw Aaaaaaaa aw Ndikupepesa pa zonse zomwe ndinachita Ndikupepesa pa zonse zomwe nnakulakwira Ndikupepesa pokunamiza kuswa mtima wako Ndikupepesa pomkhala mkaz yomwe suna fune Ndipanga chilichose kut ndiloweso malo Ndipanga chilichose kut nd loweso malo

Sharing is cool

You may also like...



Mobile Site

To view this page on the Malawi-Music.com mobile site Click here

Review

Comments
Hits 2655 Plays. | 2019 Downloads.

Follow Malawi Music on Instagram