Vote For This Song
Lyrics
INTRO Haaaaa! Swazilicious Odick! HAHAHAHAH!!!!! Ndakumana ndi Jane dzulo koma ngati andimanga ma chain, ine kufuna kulowa pansi Ndinchaka amanditcha!!! HOOK Amanditcha swazi ,ama! Amanditcha swazi!Zamababie sindimatha n’chaka amanditcha swazi! ama! Amanditcha swazi!x2, Zamababie sindimatha n’chaka amanditcha swazi, Ndimafuna, (nditakhala Nswati)x2 Ma Babie anandilaka n’chaka amanditcha swazi! ama! Amanditcha swazi!x2, Zamababie sindimatha n’chaka amanditcha swazi!
VERSE ONE Ndine Robort,Cyborg infact ndine swaziNdikavaila ma hope okha amangonditcha blazi Akazi omwe ndavaila akhoza kukwana track Mababie amandikana ati ndine wachi tradi Man thokani zina zama babiezi mayazi Kuthoka ndimafuna koma munthune manyazi Mu class yama swazi amanditcha kuti Ngawzi Amanditcha swazi zinalina wansembe! (BRIDGE) Mfana ochibanda wamalooks ngati wa reggae Am not that handsome but am so sexy, Ndine swazi wa default ma babie anandilaka, Mu level yama swazi am lapping up the ladder! Chick ikandikana ndimapeleka ma khatcha! Ma chick amasiku ano amangofuna ma kwacha! Amafuna Blackberry, House, Car komanso Mphasha! Ndimangoti kagwele uko kulibwino nzafe Bachelor!
(HOOK)
VERSE TWO Amanditcha swazi, mdani wachi terminator,Ndine swazi akazi kwa ine ndima predator. U can’t seduce me coz ama go-getter, Ndikusopasopa nga-ngati m’bulu wa yogeter. Ndine swazi! zinalina mfana wazipika Chick ikandijaila ndimaiwuza zipita! Mental ikabeba sindisiya ndima spita Mababie ali mbwee! Koma mfanayo ndiouma basi! Mfana osatopa 90 minute ndingo warmer basi! (Kubunyula) Ndine ouma gwa! Ngati actor wa war bus! Zamiyendo iwiri sindimadya ndikunenatu Mathanzi! Mababie akuti sindimato-to-to-to tha zinthuzi Papalazi busy on the line kundito-to-tola Zithuzi! Kukanidwa ndi Chick kwaineyo man sinkhani Chick ikandilola madoro amangobwela ndiphazi Zikamatero choncho ndiye mukuganiza ine ndingatani?
(HOOK)
VERSE THREE A wanna have Akazi five ngati ZumaNDIYE BVUTO NDI CHANI? Ati akazi amaluma! Am so rigid ngati Nsomba yodumwa! Ndine mfana ouma gwa AKA kwale HIV ili kutali ine sindingadwale, Zachibwenzi mayazi tizangopeza Chick ndi marry! Or ndizagwila miss Malawi Faith Chibale! Ndinayamba ku hopela ndili ku Nusery, Mpaka chickyo inagwidwa tli ku Secondary, Pano ku college koma ku hopela ku primary! Oh-Hooo! I don’t think am normal! I know! kukhala ndi Chick ndizikhomo! Ngati uli Swazi zimangofuna kubvomeleza! Kunama kuti uli nayo Chick ndie kusokoneza! Just be patient maybe uzabooleza! 40 years opanda Chick man mwandifooketsa! HOOK X3 THE -END |
Songwriters
Odick, EdokissSharing is cool
You may also like...
Mobile Site
Review
Swazi is a song about men who are unable to be in love because they cannot muster enough courage to approach women.
Comments
