Vote For This Song
Lyrics
Verse one Anthu ena ndi dzilombo, Ukangoiphula mpamene waputa nkhondo Ayiwala nawo ndi dongo Atamenya hustle nawo angafike pompo Alimbikira kumenya maupo kubindikira kukupempherera down fall Ayiwala mulungu si munthu awa amvabe kuwawa Bridge Asiye athoke Koma nje usafoke Poti adzasintha nkhope Likamukwanira la forty Adzadya matope Zidzatha dzilope Nde adzasintha nkhope Likamukwanira la forty HOOK Forty x3 Limakwana la forty Forty x3 Lidzakwana la forty Verse 2 Akuyuza Facebook Kuwauza anthu ati iwe wa Duu Ati ulibe kanthuuu Kumenya ma comment kumaseka with fools Kumachulutsa ma excuse Sakugwira ntchito angokhalira booze Munthu koma maganizo ngati mbuzi Chifukwa chakeno they still loose Bridge Asiye athoke Koma nje usafoke Poti adzasintha nkhope Likamukwanira la forty Adzadya matope Zidzatha dzilope Nde adzasintha nkhope Likamukwanira la forty Hook Forty x3 Limakwana la forty Forty x3 Lidzakwana la forty |
Songwriters
Piksy, BFBSharing is cool
You may also like...
Mobile Site
Review
Comments
87258 Plays. | 81667 Downloads.