Vote For This Song
Lyrics
Kumbire adanka nawo / Palibe akanakhonza / Anasiya pa dzuwa anawo / Anayesa ndi malodza /Ankati satana / Wakhala pa nsana / Kuyamba kudana / Kufuna kuphana Kuthana / Nzosauzana / Nthawi yakwana / Buluzi wa easy chitseko cha mpana CHORUS Anapita ndi nyanga zomwe kumanda / Anapita ndi nyanga zomwe kumanda / Ayo Tsoka Liyenda / Ayo Tsoka Liyenda Bambo awa anali chikhwaya / Ana moyo wawo sanamve kuwawa / Ku school akapita amathawa / Zinavuta ndi za nchere analawa / Yes Sanauzidwe za moyo / Anapeza bwanji makolo/Chuma/Moyo unakoma/Opanda zo khoma/Kupeza izo afuna/Ohh dzi ana ulesi/Bambo awo atsamira nkono Akuti zonsezi /Ndi curse/Chayabwa chitedze/Mavuto pang'ono see they stressed/ CHORUS Mudziwaphunzitsa ana/SiKupangira pa mawa/Asamayese ngati ophweka moyo/Mukadzapita adzakhala akapolo/ Musama yiwale/Kuti zanu munapanga kale/Nzeru zanu sizingatsale/Mungadzavutitse abale/Mdzakolola zomwe mudzale/Chuma ichi sangasamale/Ngati panopa simuphunzitsa/Mapangidwe ake mukumpusitsa/Tsoka ilo CHORUS |
Songwriters
PiksySharing is cool
You may also like...
Mobile Site
Review
Piksy is back! New single, and new album on the way.
