Vote For This Song
Lyrics
INTRO Foxxy i see you Piksy Ayeee ena adzatsalaa VERSE ONE Mboba osaphweketsa Game pa mwamba osadekhetsa Fanz yavaya utsala wekha Ukapusa sudzawapeza Siukudabwa akum'feela neighbor Ndeno madolo aku pretender Timawadziwa nde tingosetha Kutinamiza they doing better CHORUS Mukumva bwanji mnthupi? Chonchobe Bwanji mwavala Juzi? Chonchobe Ma post timawaona mboba Oh sorry Timadziwa kuti mukunama koma Chonchobe Mukumva bwanji mnthupi? Chonchobe Bwanji mwavala Juzi? Chonchobe Ma post timawaona adona Oh sorry Timadziwa kuti mukunama koma Chonchobe VERSE TWO Akuchita kuvala mbina Awonekeko bho pa picture Kukumana naye ndi munthu wina Koma iyi ndi nkhani ya tsiku lina Pa social media mboba simunama (Ndinu bwana) Kukhalira kunamiza atsikana (Mumakwana) Koma Ayeee ena adzatsala Nokha mupeze ma ansala CHORUS Mukumva bwanji mnthupi? Chonchobe Bwanji mwavala Juzi? Chonchobe Ma post timawaona mboba Oh sorry Timadziwa kuti mukunama koma Chonchobe Mukumva bwanji mnthupi? Chonchobe Bwanji mwavala Juzi? Chonchobe Ma post timawaona adona Oh sorry Timadziwa kuti mukunama koma Chonchobe VERSE THREE Kupanga tweet kutchila ndi ma dada Ku mount soche muli pa Zode (Zodetsa) Kutenga selfie ma chills ndi my girls Ku Four Seasons muli pa Mbowe Mukumva bwanji Mthupi Chonchobe Ayeeee ena adzatsala Mboba osaphweketsa (ndinu bwana) Nokha mupeze ma ansala |
Sharing is cool
You may also like...
Mobile Site
Review
Comments
52226 Plays. | 123297 Downloads.