Vote For This Song
Lyrics
VERSE ONE Kumata kumata ndi superglue Uli duu Kuutolatola mtima wanga pansi uli mbuu Kumata ndi bostic Mbali zonse kuchta stick 2getha wambawamba osamvetsa yako logic Unali wanga driver So loyal to me sunasamale nkhan zomwe unazimva Kundimatilira maso ako pa future Kunali chi mdima koma unkadziwa kucha. Kundisekerera Nkamazima kupemelera Moyenera Kundinyengelera mpaka ntakolera Sizinkabisika nanenso ndinkahopela Koma kugwa muchkondi simmene ndinkaopela. Ngati kabebe unandilera. Ikamagwa mvula unali umblera. Zomwe unamatazi sizingatheke kumatula. Chikondi chako ndalama sizingathe kugula. CHORUS Unatola mtima wanga uli wosweka, ulibe mantha Mmene ena anaseka, nati ndatheka unanditsata Unamata-mata-mata-mata-mata-mata mtima wanga Mtima wanga unawina Sindingampatse wina VERSE TWO Yako fandum Ngat yochita kupanga zoom Ndikondwa mudzi wako onseu ndine mfumu Unamatamatako konse sunasiye room Ena kumayesera kuti alowe koma hmmm? Ndimakondwera ndikamaona ka view. Nde iweyo ameneyo everyday u look brand new Ndichikondi chako chomwe chindipatsa mphamvu Zonsezi in one sentence honey i love you Kukusiya iwe ndikuluza timing Poti munyengo yaziphaliwali u stood by me In so doing unawina chikondi cha ine Mpaka muyaya ndiri nawe n'patse poti nsaine. Unakhulupira mwa ine kuchoka pa chyambi Ndisanapsetsetse ndikumveka khambi. Pano ndapsano umveno ku-kukoma kwa changachi chikondi udzingopanga download. VERSE THREE Mu mvula ya ziphaliwaliwali unandikonda more Kumangofeela warm – kumangofeela bho Kuthamangitsa zinthu zanga zikamayenda slow Kumangofeela bho – kumangofeela bho Si inenso wamanyazi sweetie you make me stand tall Kumangofeela bho – ine kumangofeela bho Usiku usanagone kundimenyera ka call Kumangofeela bho – kumangofeela bho
|
Songwriters
Evans "Nthumwi Piksy" ZangazangaSharing is cool
You may also like...
Mobile Site
Review
Maso Songs | Ponya Mwendo » |