Vote For This Song

Lyrics

Phee!! Lyrics Artists: Phyzix ft. Macelba Album: ...Of the Highest Order EP. Producers: Dare Devilz & Stich Fray Label: It’s Only Entertainment (IOE) (Intro: Phyzix & Macelba) Phee!! Phe!!/ Very Good Very Good/ We Here! (Prelude: Phyzix) La/ La La La La La La La La La La La La/ ndife afana otentha La La La La La La (Verse 1: Phyzix) Naturally ndine starbwoy/ am a smoking hot king sikuti m’masuta gway/ haters wonder why am still a top guy/ amandinyoza kumbali pa maso akuti hie/ ndimadana m’macheza opusa bye bye/ musamapange zanu za tulo ndi ineyo ayi/ Ndimachita manyazi kuluza am shyi/ am a born winner pita ukafuse amayi/ ine sindIzaLALA sindili ngati boat/ Flow yanga bima ma rappers ndi ma note/ Ineyo kuzatha ndi mulandu wa ku khothi/ wondiputa sangandimalize Nsanje Port (Hook: Phyzix) Olo mukhomelere/ Phee!! Olo ndizidya thelere/ Phee!! Ndife mafana o’riser basi/ timasongola mu minibus/ Phee!! Olo mukhomelere/ Phee!! Olo ndizidya thelere/ Phee!! Ndife mafana otentha basi/ Kuphaka life ndi pin basi/ Phee!! (Verse 2: Macelba) Mfana otentha mboni yanga ndima hit Ndanyowetsa machesi mulimbilana chilibiliti Kundizizilitsa sizitheka Ndine virigo pa beat funsafunsa sindidyeka Ndizizila bwanji anzanga ndi ma hitmaker Fanz inkakukwera kale pano unatha double decker Anzanga ine ndi 5 okha Enanu ndiongonamizana nkhani ngati 5 moba Ndimakolera nanji mkandithira fire American height koma m’chimfana chaku kaya Mukutolera nkhuni nthawi yoipatsa moto Iyiyi ndi real sound ya achina skeffa chimoto (Hook: Phyzix) Olo mukhomelere/ Phee!! Olo ndizidya thelere/ Phee!! Ndife mafana o’riser basi/ timasongola mu minibus/ Phee!! Olo mukhomelere/ Phee!! Olo ndizidya thelere/ Phee!! Ndife mafana otentha basi/ Kuphaka life ndi pin basi/ Phee!! (Bridge: Phyzix) La/ La La La La La La La La La La La La/ ndife afana otentha La La La La La La (Verse 3: Phyzix) Am about to ruin your day/ ndikafika pamalo fanzi imafila tonde/ oh yeah/ u dolo wanu uli panja simungalowe munomo mumathela khonde/ all day/ I smell something fishy ngati bombe/ mafanawa ngoipa akufuna andinyonge/ Munditenge bwinotu ineyo Mundihonge/ muzindipatsa ma very good mundichonge I work hard on MINE/ ndi kayelekela/ mafana ondigwetsa si m’mene amalephelera/ amafuna kundisala ngati wakudela/ simungandigonjetse ndinabwera (Hook: Phyzix) Olo mukhomelere/ Phee!! Olo ndizidya thelere/ Phee!! Ndife mafana o’riser basi/ timasongola mu minibus/ Phee!! Olo mukhomelere/ Phee!! Olo ndizidya thelere/ Phee!! Ndife mafana otentha basi/ Kuphaka life ndi pin basi/ Phee!!

Sharing is cool

You may also like...



Mobile Site

To view this page on the Malawi-Music.com mobile site Click here

Review

Comments
Hits 2201 Plays. | 34711 Downloads.

Follow Malawi Music on Instagram