Vote For This Song
Lyrics
(Verse 1: Phyzix) Akubwera ndi chigulu cha mipaliro/ ndikapanga zibwana nthokhala maliro/ akufuna zake komano date yo/ ndizitenga kutiko zobweza la lero/ akuchita kukuwa kuti iwe na lero/ tikufinya finya utuluka za yellow/ ndimafuna kuthawa ati gwirani Mani yo/ akuti andiyalutsa andijambula-video/ ndizichita kuveka mau anga pa-audio/ kuti kape uja zamuthina kuno/ tachita kumutulutsa blood mphuno/ timulanda zovala ayenda buno/ aphuzire kumadya ndalama bwino/ sizikutuluka wamba Boma lino/ pa Ground sipali bho/ no malido/ panopo sitikumadya nkhomaliro/ eh (Hook: GD) Ndikumayenda cha mpeni/ zweee Asandipeze pa den/ No No No Akumabwera ndi zi mipeni/ Zi agalu atazimanga ku matcheni Pa Ground sipali bho/ No No No Pa Ground sipali bho/ No No No Pa Ground sipali bho/ No No No Pa Ground sipali bho axe ndi black tax/ chilungamo chake panopo life sucks (Verse 3: GD) Bebi yanga wandilanda blesser/ sizimandiwaza zoti ngini izindi stresser/ ndikumenya goals iwe busy kupatsa pressure/ ndikumva kuwawa ngati drink yopanda chaser/ pa ground sipali bho player akungotelera/ izi ndi zenzeni awawa si masewera/ ine ndilibe kanthu ngati truck yopanda telera/ one by one ngati mwana akudya cerelac (Verse 4: Marcus) GD/ mabwana sakulipira/ maluzi andipha olo mkazi sakulilira/ Landlord mpaka 5 missed calls/ m’town ndilimba?/ kupanda Prophet ndi masten bwenzi ine ndili ndani/ ndadzala mitengo koma osafetsa/ simdzatenganso katapila adzandiphetsa/ mwina ndiyambe Pente ndisiye mu Mpesa/ Pa Ground ndithana napo mwazi ndiukhetsa |
Sharing is cool
You may also like...
Mobile Site
Review
Phyzix takes the Daredevilz on another song as the trio stresses the current economic hardships using the trending phrase "Pa Ground Sipali Bho."Comments
