
Phyzix
Chitsanzo ft Danny Kalima (Prod by Dare Devilz and BFB)
Gamba Wa Yesu (2015)
Tags Gamba Wa Suit Gamba Phyzix Danny Kalima Gamba Wa Yesu
Vote For This Song
Lyrics
-Intro- Yeah Iwe ndi uti? Gamba wopemphera/ C'mon! Yeah, Phyzix Danny Kalima -Hook- Ngati ndaborna winawake aborna Ngati ndasintha winawake asintha Ngati ndamudziwa Yesu/ amudziwa Yesu Amandiwelenga ngati ndine bukhu Mafanawa/ Mayuthiwa Ndikhale ndikhale Chitsanzo cha bho Cha mafanawa/ Cha mayuthiwa Ndikhale ndikhale Chitsanzo cha bho! - Verse 1 - (Phyzix) Amandidziwa/ Nsanje to Chitipa Nyimbo ya Cholapitsa inanditchukitsa Tsa/ Tsa/ Tsa/ Ine ndine Phyzo Sikuti ndisintha dzina poti ndinaborna Ndimadziwa ntchito zanga ndi zonyasa Ndine munthu wolephela ndine wochimwa Grace/ Grace// chisomo cha Ambuye Ndichomwe ndikufuna kuti mwina ndingalimbe Ndichilitseni/ Ambuye dalitseni Muwapatse moyo wautali Amayi/ Masten Dziko/ ndi lovuta Moyo/ ndi wozunza Timafuna winawake a role model woti zake zikuyenda/ akuwina nkhondo Si Yudasi/ si Jemusi/ si Phyzix Ndi Yesu basi -Hook- Ngati ndaborna winawake aborna Ngati ndasintha winawake asintha Ngati ndamudziwa Yesu/ amudziwa Yesu Amandiwelenga ngati ndine bukhu Mafanawa/ Mayuthiwa Ndikhale ndikhale Chitsanzo cha bho Cha mafanawa/ Cha mayuthiwa Ndikhale ndikhale Chitsanzo cha bho! - Verse 2 - (Phyzix) The Real Elements/ Q/ Marvel Plan B/ Stix/ anandipatsa chitsanzo Kuti Hip Hop idzimveka ngati Nyambo Akupitilizabe kundipatsa chitsanzo Anakula Anaborna Anakwatila Ndinakula Ndinaborna Ndikukwatila Mbali yanga ngati M'khristu ndipange Dziko sadzaliwononga ndi madzi Moto kuupewa ndikulapa tchimo Kumapemphera kumawelenga baibulo Kumasonkhana ndi anthu/ Mpingo Mundipatse mtima wodzichepetsa Mzimu woyera tchimo muzindiletsa Kutchuka kwanga kuzilemekeza inu Chuma changa chakhumi kupatsa inu Ndidzikonda momwe mukondera inu -Hook- Ngati ndaborna winawake aborna Ngati ndasintha winawake asintha Ngati ndamudziwa Yesu/ amudziwa Yesu Amandiwelenga ngati ndine bukhu Mafanawa/ Mayuthiwa Ndikhale ndikhale Chitsanzo cha bho Cha mafanawa/ Cha mayuthiwa Ndikhale ndikhale Chitsanzo cha bho! - Verse 3 - (Danny Kalima) Amayi anati/ opanda Yesu sungakwanitse Amayi anati/ ugwiritsitse Yesuyo Lero ndakonzeka kusintha moyo wanga Munayamba kale kundiyitanaaaaa! - Verse 4 - (Phyzix) Mulungu wanga ndabwera pamaso panu Mundikhululukire zochimwa zanga Ambiri zawasocheletsa nyimbo zanga Ndikupepesa/ Ndikupepesa Ngati mungakhululuke/ Ndapepesa Ndikufuna mwana wanu/ Yesuyo Ali mkono wakumanjayo/ Yes uyo Sindidzamukana olo ngati Petulo -Hook- Ngati ndaborna winawake aborna Ngati ndasintha winawake asintha Ngati ndamudziwa Yesu/ amudziwa Yesu Amandiwelenga ngati ndine bukhu Mafanawa/ Mayuthiwa Ndikhale ndikhale Chitsanzo cha bho Cha mafanawa/ Cha mayuthiwa Ndikhale ndikhale Chitsanzo cha bho! -Hook- Ngati ndaborna winawake aborna Ngati ndasintha winawake asintha Ngati ndamudziwa Yesu/ amudziwa Yesu Amandiwelenga ngati ndine bukhu Mafanawa/ Mayuthiwa Ndikhale ndikhale Chitsanzo cha bho Cha mafanawa/ Cha mayuthiwa Ndikhale ndikhale Chitsanzo cha bho! -Outro- Thank you Jesus Forgive me all of my sins I make you my Lord and Saviour Amen. J.E.S.U.S Jesus! |
Sharing is cool
You may also like...
Mobile Site
Review
Comments
