Vote For This Song
Lyrics
*NAZO Lyrics by Phyzix* *INTRO* Politics/ Conflicts/ Mabebi/ Maluzi Politics/ Conflicts/ Mabebi/ Maluzi *VERSE 1* Ndimadya thukuta langa/ ndine chimfana cha umve/ zachibwana sindimapanga ndine kapolo sanakuuze/ tanena kuti tikumve zomwe zimavuta kuti utimve/ ndife mafana a kalekale tinawerenga Tsala ndi Timve/ ma vote nde timaponya koma tikumadyabe zi bonya/ a ndalewa ndi mabebi ndi amene akumapanga zobhowa/ amabwera ndi ma heart break mphwanga utha kuphowa/ zikati zafika mbola palibe zokuti ndiwe chiphona/ ndatopa nazo *HOOK* Ndatopa nazo/ ndatopa zazo Ndatotopa nazo nazo Ndatopa nazo/ ndatopa zazo Ndatotopa nazo nazo Politics/ Conflicts/ Mabebi/ Maluzi Politics/ Conflicts/ Mabebi/ Maluzi *VERSE 2* Sizikupanga chipongwe anthu panopo si zi kufwamba/ ndatopa kuphula njerwa ndikufuna ndizatole chikwama/ struggle mu ghetto si ti ma kazinga chakudya timawilitsa/ water mu kettle ku yi khwidzinga kenako madzi kuphitsa/ ukwati wa dzulo uja kucha kwa lero akuti watha/ ndalama za chipatala zija akuti aba zatha/ zaka zaka zikupita koma moyo osamasintha/ bolanso weather umadziwa kuti summer kenako winter/ ndatopa nazo *HOOK* Ndatopa nazo/ ndatopa zazo Ndatotopa nazo nazo Ndatopa nazo/ ndatopa zazo Ndatotopa nazo nazo Politics/ Conflicts/ Mabebi/ Maluzi Politics/ Conflicts/ Mabebi/ Maluzi *BRIDGE* Ndatopa nazo/ ndatopa ndatopa zazo *HOOK* Ndatopa nazo/ ndatopa zazo Ndatotopa nazo nazo Ndatopa nazo/ ndatopa zazo Ndatotopa nazo nazo Politics/ Conflicts/ Mabebi/ Maluzi Politics/ Conflicts/ Mabebi/ Maluzi |
Songwriters
Noel "Phyzix" Chikoleka, Beat Bear, Stich Frey, Richard BillySharing is cool
You may also like...
Mobile Site
Review
Comments
